13/08/2026
Nkhani yovetsa chisoni😭💔
*Uthenga wa maliro*
Abusa a Mazoni omwe akhala akudwala kwa ka nthawi, Atisiya.
Program yose ya mwambo wa maliro ikadziwika, tikudziwitsani.
Mzimu wa abusa a Mazoni, uwuse muntendere!🙏🪽🪦