Mlima CCAP church

Mlima CCAP church Preaching the Word of GOD till the second coming of Jesus christ

Tikumane mawa 8koloko madzulo
30/12/2024

Tikumane mawa 8koloko madzulo

Uthenga ndi umenewu
27/12/2024

Uthenga ndi umenewu

24/12/2024

Mwaswera bwanji pamudzi pano,mawa paja ndi 25 December, Christmas day,tikumbukire kuti mawa service ilipo Ku Church, nthawi ya 8koloko mmawa,tiyeni tikamulambire ndi kumkweza

14/09/2024

Mapemphero akusalakudya

Mwaswera bwanji pamudzi pano?Tidziwitse kuti mawa kuli mapemphero osala kudya.Nthawi ya 8am mpaka 4pmMalo:Mlima CCAP.Com...
13/09/2024

Mwaswera bwanji pamudzi pano?
Tidziwitse kuti mawa kuli mapemphero osala kudya.
Nthawi ya 8am mpaka 4pm
Malo:Mlima CCAP.
Come one come allows

07/09/2024

Mwaswera bwanji pamudzi pano?

Mawa ndi Sunday ,ndiye kuti mmawa musadzatanganidwe konzekeranitu lero,kaya zovala sitiramtuni mkuyika pabwino,nsapato Ku polishiratu.mukatero basi mudzingodikira mawalo.

Ambuye akudalitseni

06/09/2024
Koma Sunday kunayaka motoπŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ’¨πŸ’¨,Steve chitanda what a show,what a wonderful launch
03/09/2024

Koma Sunday kunayaka motoπŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ’¨πŸ’¨,
Steve chitanda what a show,what a wonderful launch

Mtsonkhano wa chigwirizano cha amayi Ku chikungu CCAP wayenda bwino.Ambuye alandire ulemu.
12/08/2024

Mtsonkhano wa chigwirizano cha amayi Ku chikungu CCAP wayenda bwino.Ambuye alandire ulemu.

Tiyeni tikapemphere
11/08/2024

Tiyeni tikapemphere

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mlima CCAP church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share