Kubadwa mwasopano mwa mbuye

Kubadwa mwasopano mwa mbuye Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Kubadwa mwasopano mwa mbuye, Full Gospel Church, Lilongwe.

CHIVUMBULUTSO 2 : 21Ndipo ndampatsa iye nthawi kuti alape; koma safuna kulapa kusiyana nacho chigololo chake.For read mo...
01/07/2024

CHIVUMBULUTSO 2 : 21

Ndipo ndampatsa iye nthawi kuti alape; koma safuna kulapa kusiyana nacho chigololo chake.
For read more download the Bible using this link:

MATEYU 12 : 12Nanga kuposa kwake kwa munthu ndi nkhosa nkotani! Chifukwa cha ichi nkuloleka kuchita zabwino tsiku la Sab...
01/07/2024

MATEYU 12 : 12

Nanga kuposa kwake kwa munthu ndi nkhosa nkotani! Chifukwa cha ichi nkuloleka kuchita zabwino tsiku la Sabata.
For read more download the Bible using this link:

YEREMIYA 29 : 11Pakuti ndidziwa malingiriro amene ndilingiririra inu, ati Yehova, malingiriro a mtendere, si a choipa, a...
29/06/2024

YEREMIYA 29 : 11

Pakuti ndidziwa malingiriro amene ndilingiririra inu, ati Yehova, malingiriro a mtendere, si a choipa, akukupatsani inu adzukulu ndi chiyembekezero.
For read more download the Bible using this link:

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kubadwa mwasopano mwa mbuye posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share