St paul's anglican youth, chilinde parish

St paul's anglican youth, chilinde parish Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from St paul's anglican youth, chilinde parish, Religious organisation, P. O Box 20188, kawale, Lilongwe.

22/03/2016

archdeaconry youth conference on 15-17 April, 2016 at st Paul's Anglican, chilinde parish, mwakonzeka

08/12/2015

Tikumbutsane k*t Saturday pa 12 December, tukayendera anzathu ku chipatala cha bwaila ndiye tiyen tonse tikapezane ku Church time yabwino k*t tikavwerenso time yabwino, Ambuye akudalitsen

Photos of the year at 2015 diocese of lake Malawi, youth rally, ntchisi
03/12/2015

Photos of the year at 2015 diocese of lake Malawi, youth rally, ntchisi

27/11/2015

Tikumbutsane k*t pa Sunday 29 November, 2015 tikupita ku Christ the king ndiye tiyen tonse mwaunyinji tikapezane komweko, tikawachezere anzathu

14/11/2015

Today's program is kuyendera ofooka ku KALIYEKA, tiyen tibwere mwaunyinji tikawatenge anzathu k*t za Ambuyezi zisawapophonye

09/11/2015

Mulungu anapatsa koma Mulungu yemweyo watenga lidalitsike dzina lake mzimu wa mayi kafumba ndi bambo majawa iwuse mu ntendere

rest in peace tessa
28/04/2015

rest in peace tessa

07/12/2014

we are the champions

captain & vice captain kuuzana zoti wina akhale m`busa
03/04/2014

captain & vice captain kuuzana zoti wina akhale m`busa

10/03/2014

Youth group football team
yayambanso & now pozindikira k*ti palibe chaulele training allowes iziperekedwa

12/10/2013

tikufuna timve maganizo anu pa zithu izi
1. Pa ulendo wakunyanja, kodi mufuna tikakhaleko masiku angati & tipite nyanja yambali yak*ti?
2. Kodi youth day ikakhalire k*ti ngati ilipo?
3. Kodi youth yathu ikuyenda kapena ayi?
Pelekan maganizo anu admin amve & k*ti tithandizane

11/10/2013

morning

Address

P. O Box 20188, Kawale
Lilongwe
LILONGWE

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when St paul's anglican youth, chilinde parish posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share