Nanjiri Assemblies Of God

Nanjiri Assemblies Of God We Are The Church Under Malawi Assemblies Of God

Happy Birthday to our own... Mayi Busa
12/08/2021

Happy Birthday to our own... Mayi Busa

02/08/2021
18/07/2021

No other nation has ever changed its gods, even though they were not real. But my people have exchanged me, the God who has brought them honour, for gods that can do nothing for them.
Jeremiah 2:11 GNB

12/06/2021

Mwaswera bwanji?

1 Kodi moyo wanu wa uzimu ukukula?
2 Kodi mungadziwe bwanji kuti moyo wa uzimu ukukula?

Mafuso amenewa ayankhidwa mu uthenga wa mawa. Tiyeni tibwera musunga nthawi

Theme: "INDICATORS OF SPIRITUAL GROWTH"

31/05/2021

Haman, became a victim of his own plot.
His plans against the Jews and Mordecai boomeranged.
Whatever plot that is conclude and signed against you and your household this season is frustrated.
There shall be total liberation from all attacked in Jesus Christ Name. Isaiah 54 vs 17.
Happy New week

30/05/2021
27/05/2021

Tikanena kuti tilibe tchimo, tikudzinyenga tokha ndipo mwa ife mulibe choonadi. Koma tikavomereza machimo athu, Iye ndi wokhulupirika ndi wolungama ndipo adzatikhululukira machimo athu, nadzatiyeretsa ndi kutichotsera chosalungama chilichonse. Ife tikanena kuti sitinachimwe, tikumutenga Mulungu kukhala wonama, ndipo Mawu ake sali mwa ife.
1 Yohane 1:8‭-‬10 CCL

Kodi ndi tchimo liti lomwe likuzuza moyo wathu?

Masiku ana anthu tikufuna kulambira Mulungu koma tikuchitabe machimo malo obisika, monga chigololo, miseche, kuba, chinyengo, bodza, nsanje, dziwani Mulungu akukuona zinafunika mulape mwasanga. Lero Mulungu wakupatsani mpata ku mukoze moyo wanu.

Tsiku lopambana

26/05/2021

Adzakuphimba ndi nthenga zake, ndipo udzapeza malo othawira mʼmapikomo; kukhulupirika kwake kudzakhala chishango chako ndi lihawo. Sudzachita mantha ndi zoopsa za usiku, kapena muvi wowuluka masana, kapena mliri umene umayenda mu mdima, kapena zowononga za pa nthawi ya masana.
Masalimo 91:4‭-‬6 CCL

*Mukhale ndi usiku wopambana*

25/05/2021

Pakuti mkwiyo wake umakhala kwa kanthawi koma kukoma mtima kwake ndi kwa moyo wonse; utha kuchezera kulira usiku wonse, koma chimwemwe chimabwera mmawa.
Masalimo 30:5 CCL

Landirani chimwemwe mu dzina la Yesu!

Sunday things
17/05/2021

Sunday things

17/04/2021

May God advance you in every area of your life.
Mercy will always speak for you.
You are exempted from undue delay and unnecessary denials, disgrace or disappointments.
Your expectations and desires will not be cut off.
The God of suddenly will prove Himself mightly in your life.
God will fight for you and you shall hold your peace.
Happy weekend to you friends.

Making progress
06/04/2021

Making progress

Address

Lilongwe

Telephone

+265881554301

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nanjiri Assemblies Of God posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share