Kasungu church of chrust

Kasungu church of chrust Am always busy busy on WhatsApp Facebook Twitter and Instagram email is [email protected] WhatsApp is +265996571746 Facebook Praise Blyson

10/08/2023

+265998028844 whatsapp number

01/12/2021

Hello brother s and sister s

21/06/2020
22/05/2020

Tsiku labwinono kwa nonse abele anga ndiyalongo komwe muliko, ndilandileni rero pamene tikufuna tikumbusane, kuphuzitsana ndikudziwitsana mawu ake. Tiyeni tione buku la Detronomo 12 vs 1. Yehova mulungu analikuchenjeza ana aislael pak*t anawona anaayislael atatayilira mchipembedzo nayamba kulambi milungu anawauza k*t malo oyera akhale amodzi onongan malo onse omwe amitundu akulambilako mafano gwetsani maguwa awoansembe nifufute mayina awo achoke. Yehova tikaona anakana k*t dzinalake lichoke mmalomwake amankafuna dzinalomwe analikhazikisa likhale lomwelo lomwe anthu azililambila kmaso malo omwe anasakha akhare omwewo athuazikakumanako ndkulambilako dzinalake chifukwa tikaona vs ya 3 ak*t dzichenjeraninokha musamapereke sembe maupi anu palipose mupaona km pamene nddzasakha mwamafuko anu pamenepo muzifunako ndkufikako. Dzakhalen pomwepo pamene tikupitiriza phuziro lathu nthawiyina ambuye akudalisen amen.

25/04/2020

Ndikulandleni abale ndyalongo nonse komwemuliko dziwani k*ti yehova amakukondan koposa pokupangani k*ti mukhale ndmoyo kufikira pomwemulipo , sonondichithu chonyadilisa kwayiye mutamavera mau ake ndkuwachita poti ichi mchimene iye afuna, khalani pomwepo pamene tikhala tikusathula mawu ake mnthaw ikubwerayi ambuye akudaliseni nonse amen.

30/03/2020

Mathews 16:18 Jesus buld his church

20/11/2019
05/11/2019

Mathews 16vs18

02/11/2019

God is Great

01/11/2019

Am always busy busy on WhatsApp Facebook Twitter and Instagram email is [email protected] WhatsApp is +265996571746 Facebook Praise Blyson

Address

Praise Blyson
Lilongwe
NA

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kasungu church of chrust posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Kasungu church of chrust:

Share