29/08/2026
MAWA MUKAPEMPHERA KUTI?
Ife ku parish yathu tili ndi Chaka cha Ukalistia pamene ana akhale akuyamba kulandira sacrament la Ukalistia
Misa izakhalapo imodzi nthawi ya 7 koloko mmawa
Ngati mungathe, bwerani muzapemphere nafe komanso kuzasangalala limodzi ndi ana athu pamene akuyamba kulandira ukalistia...