Coptic Orthodox Church, Malawi

Coptic Orthodox Church, Malawi Coptic Orthodox Church

"When God's contentment dwells in our hearts, everything becomes more beautiful.""Pamene mtendere wa Mulungu ukhala m'mi...
25/08/2026

"When God's contentment dwells in our hearts, everything becomes more beautiful."

"Pamene mtendere wa Mulungu ukhala m'mitima yathu, chilichonse chimakhala chabwino."

Every word we speak is a seed planted in a person's heart; it will either bear fruit of peace and joy, or leave behind b...
24/08/2026

Every word we speak is a seed planted in a person's heart; it will either bear fruit of peace and joy, or leave behind bitterness and pain.

Therefore, we must be mindful of our words.

"Mau aliwonse amene timanena ali ngati mbeu yomwe timafesa mumtima mwa munthu; Ikhonza kubala zipatso za mtendere ndi chimwemwe, kapena kusiya zowawa ndi ululu

Choncho tiyenera kusamala ndi mau athu."

It's not just about saying *I am a Christian* but about people seeing Christ in my words, in my actions, and in times of...
23/08/2026

It's not just about saying *I am a Christian* but about people seeing Christ in my words, in my actions, and in times of hardship and trial.

"Sizokwanira kungonena kuti ndine Mkhristu. Anthu ayenera kuona Khristu m'mau anga, m'zochita zanga, komanso mu nthawi yamavuto."

Thursday, August 20, 2026A spiritual and recreational day for children entitled “My Path” was held in Malawi, which incl...
23/08/2026

Thursday, August 20, 2026
A spiritual and recreational day for children entitled “My Path” was held in Malawi, which included a number of features and activities aimed at developing children.

Lachinayi, pa 20 August, 2026
Tsiku lauzimu ndi losangalatsa lotchedwa "Njira yanga" linachitika ku Malawi. Linali ndi zochitika zosiyanasiyana zofuna kukuza moyo wamwana.

"True transfiguration does not make a person run away from the suffering of others; rather, it makes them tackle these d...
22/08/2026

"True transfiguration does not make a person run away from the suffering of others; rather, it makes them tackle these difficulties through Christ."

"Kusinthika kwatunthu sikupangitsa munthu kuthawa mavuto a ena; koma kumamuthandiza kuthana ndi zovutazi kudzera mwa Khristu."

"Moses did not know that God would part the sea; but he knew that God would not abandon him.""Mose sankadziwa kuti Mulun...
19/08/2026

"Moses did not know that God would part the sea; but he knew that God would not abandon him."

"Mose sankadziwa kuti Mulungu adzagawa nyanja; koma ankadziwa kuti Mulungu sadzamusiya."

Sometimes, ignoring something is the greatest wisdom. Not every word deserves a response and not every situation warrant...
16/08/2026

Sometimes, ignoring something is the greatest wisdom. Not every word deserves a response and not every situation warrants a confrontation.

"Nthawi zina kunyalanyaza pa zinthu zina ndi nzeru yaikulu. Sikuti mawu onse oyankhulidwa amayenera kuyankhidwa, ndipo si mkhalidwe uliwonse woyenera kutsutsana nawo"

15/08/2026

Divine liturgy

"Spiritual knowledge that is not linked to action is not true knowledge.""Nzeru zauzimu zomwe sizimagwirizana ndi zochit...
14/08/2026

"Spiritual knowledge that is not linked to action is not true knowledge."

"Nzeru zauzimu zomwe sizimagwirizana ndi zochita siziri nzeru zoona"

13/08/2026


Address

Chitedze Village/M12 Road/Mchinji Road
Lilongwe

Opening Hours

Monday 08:00 - 16:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 16:00
Thursday 09:00 - 16:00
Friday 09:00 - 16:00
Saturday 09:00 - 16:00
Sunday 09:00 - 16:00

Telephone

+265885053007

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Coptic Orthodox Church, Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Coptic Orthodox Church, Malawi:

Shortcuts

Share