Livingstone monkebay CCAP

Livingstone monkebay CCAP Come and worship with us

Today we saw God who lifts the useless, lifting usMulungu okweza zonyozeka takumana nayeMulungu yemwe adakakakokolola Je...
28/01/2026

Today we saw God who lifts the useless, lifting us

Mulungu okweza zonyozeka takumana naye

Mulungu yemwe adakakakokolola Jephtah ku Tobu naye watisuzumila ndipo apitilize kukumana nanu konse komwe muli

Kuli bwino kukanidwa ndi anthu bola udzikondedwa ndi Mulungu, Jephtah abale ake adamukana koma mulungu adamuvomera

05/01/2026
Every believer will face storms in life, some loud, some long, some feel like they will never end. But the good news is ...
04/11/2025

Every believer will face storms in life, some loud, some long, some feel like they will never end. But the good news is that THE STORM CAN'T SINK WHAT JESUS STEERS. When Christ is at the helm, no wind is strong enough, no wave is high enough, and no darkness is deep enough to destroy you.

16/09/2025

Mwai Olemba anthu ntchito lero

30/08/2025

This is another day God has given us! It's a day of prayer and fasting at Livingstone

29/08/2025

Prayer and fasting day 30August 2025

17/08/2025

Livingstone CCAP says thank you guys πŸ™πŸ’•πŸ‘

Much welcome man of God let's be blessed together!
16/08/2025

Much welcome man of God let's be blessed together!

11/06/2024
11/06/2024

😭😭 NTHAWI YA CHISONI KWAMBILI😭😭

Mwachisoni kwambili ndati ndikupepeseni abale anga chifukwa chotaya wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Saulos K Chilima ndi ena onse 9 omwe adali mndegemo.

Zachitikazi ndi za chisoni chosasimbika ku dziko komaso ku mpingo wonse mwa njila ina. Tiyeni tilimbe mtima munyengo yowawitsa ngati imeneyi pamene abale athu Eni Eni atisiya chomwechi.

Mulungu samalakwitsa ndipo chikondi chake pa ife ngat dziko chidakali nafebe. Tiyeni tilile ndi chiyembekezo (1 Thesselonians 4:13-18)

Mizimu yawo iwuse mu mtendere.

Rev MW TEMBO @2024

Address

C/o Livingstonia Synod
Lilongwe
MONKEBAY

Telephone

+265999611006

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Livingstone monkebay CCAP posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Livingstone monkebay CCAP:

Share