Chikungu CCAP Nkhoma SYNOD

Chikungu CCAP Nkhoma SYNOD This is the official page for CHIKUNGU CCAP. CHIKUNGU CCAP is one of the Nkhoma SYNOD churches.

DAY 3 OUT OF 30 KUKAMBILANA ZA M'BANJANTHAWI 6PM- 8PM
28/01/2026

DAY 3 OUT OF 30

KUKAMBILANA ZA M'BANJA

NTHAWI 6PM- 8PM

26/01/2026
Join us for Sunday service s From 06:8am MUTU : Ngati tazindikira Akhristu monga mwa thupi koma tsopano sitinzindikirans...
22/01/2026

Join us for Sunday service s
From 06:8am

MUTU : Ngati tazindikira Akhristu monga mwa thupi koma tsopano sitinzindikiranso motero 2 Akorinto 5:16

Abusa a mpingowo a NES. Chimtolo ndiwo adzakhala akutumikira pa tsiku limeneli. Bwerani nonse tidzadalitsike limodzi.

Lero pa 25 December 2025 , linali tsiku la pamwamba kwambiri pamene Abusa a N.E.S ndi Amai  Chimtolo ndi atsogoleri onse...
25/12/2025

Lero pa 25 December 2025 , linali tsiku la pamwamba kwambiri pamene Abusa a N.E.S ndi Amai Chimtolo ndi atsogoleri onse a mpingowu adakonza mwambo wa padera wa madyelero ,umene takhala tikucheza,kudya kugawana nawo mau a Mulungu komaso kuwapatsa mphatso anzathu omwe ndi okalamba motsogozedwa ndi a bungwe la Zachifundo. Ngati njira imodzi yongomuthokonza Mulungu pa zabwino zimene watichitira ngati Mpingo.Ambuye akudalitseni nonse.

Mawa kumaliza mapemphero 8:00am ndipo Chidyerano chidzayamba nthawi ya 9:00am ndipo aliyese pobwera adzatenge chakudya c...
24/12/2025

Mawa kumaliza mapemphero 8:00am
ndipo Chidyerano chidzayamba nthawi ya 9:00am ndipo aliyese pobwera adzatenge chakudya chilichonse chomwe wakonza kuti adzagawane ndi anzawo. Kumeneko tidzakhalaso ndi anzathu omwe ndi okalamba komaso aulumali amene amadyera M'gonero kumadera awo.Bwerani nonse kuti tidzasangalale tonse limodzi.

14/12/2025

🔙 A year ago. Came, saw and conquered. Left an indelible mark.

RCZ

Lero Linali Tsiku lomwe Mpingo Wa Chikungu Tinakacheza Moyanjana Ndi Abusa A. Guwende Omwe adatumikorapo pa Mpingo Wa Ch...
17/11/2025

Lero Linali Tsiku lomwe Mpingo Wa Chikungu Tinakacheza Moyanjana Ndi Abusa A. Guwende Omwe adatumikorapo pa Mpingo Wa Chikungu.

19/10/2025
19/07/2025

ANNOUNCEMENT/CHIDZIWITSO 19.07.25

Mawa pa 20 July 2025 tidzakhala ndi zipembedzo ziwiri. Chipembedzo choyamba chidzayamba nthawi ya 07:00am. Chipembedzo cha chiwiri chidzayamba nthawi ya 09:30am. Zipembedzo zonsezi amene adzatsogolere ndi abusa a Lazarus Phiri omwe ayenda limodzi ndi choir ya Chivumbulutso Women's RCZ kuchokera ku Zambia. Zipembedzo zonse zidzawulutsidwa pa tsamba lino.

11 May 2025Pictorial Focus
11/05/2025

11 May 2025

Pictorial Focus

11/05/2025

Address

Area 50
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chikungu CCAP Nkhoma SYNOD posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Chikungu CCAP Nkhoma SYNOD:

Share