Masintha CCAP

Masintha CCAP P.O BOX 20142
Lilongwe
Malawi

Mulungu aliyense anampatsa nthawi yake yomudalitsila Tiyeni tiphunzile kukhala anthu odikila ndi opilira ngat team ya ar...
20/05/2026

Mulungu aliyense anampatsa nthawi yake yomudalitsila

Tiyeni tiphunzile kukhala anthu odikila ndi opilira ngat team ya arsenal yomwe yakhala zaka 22 isanawine league

Mu nthawi yake Mulungu adzakuyakhani ‭ : Jeremiah 33:3

Congratulations kwa anzathu onse okonda Arsenal

It's today💥💥💥💥 iyiyi ikufunika Live tidalitsike tonse pamodzi pano✊️✊️✊️
17/05/2026

It's today💥💥💥💥 iyiyi ikufunika Live tidalitsike tonse pamodzi pano✊️✊️✊️

Zochitika za sunday💥💫💯
16/05/2026

Zochitika za sunday💥💫💯

Ana akasambe ku Salima🤸‍♂️🤸‍♀️🤸‍♂️🤸‍♀️
15/05/2026

Ana akasambe ku Salima🤸‍♂️🤸‍♀️🤸‍♂️🤸‍♀️

Ngati mpingo tiima nanu ana athu mugawo ili mawa lino🙏🙏🙏🙏🙏🙏
01/05/2026

Ngati mpingo tiima nanu ana athu mugawo ili mawa lino🙏🙏🙏🙏🙏🙏

01/05/2026

Big shout out to my new rising fans! Elitah Pias Kafulafula, Rhodrick Jimson, Clement Richard, Rejoice Kakhobwe, Shameem Makawa, Regina Baluti Kaseko, Patricia Chisambi, George Ngalale, Hastings Kalulu, Chifundo Kasauka Rino, Wyson Mlongot, Patrick Chimpango, Feston Chigwenembe, Harriet Ngoma, James Joseph Banda, Ireen Mjambe, Josephine Danger, Alinafe DK Stephanie, Yammie Edward, Miliam Kamtedza, Maria Munyenyembe, Joyce Majonga Wa Kaponda, Chissomo Mtepatepa, Mala Babie Usufu, Save Khonje, Christina Mwale, Nancy Bvumbwe, Rose Kamunthu, Love Somanje, Blessings Suluma, Omlie Chama, Listand Phwitiko, Alfred Thomas, Mable Zuze, Thenjiwe Moyo, Malisia Kandulu Chilumba, Destiny Pastor Milton, Wizzie Kank, Josophine Ngwira, Redgie Kondwani, Peter Wa Thomas Phiri, Lucia Wa Misolo, Marcos Joaquim Menhaute, Sarah Isaiah, Stevie Bosco Chitsamba, Bwanaliti Malesh, Shadreck Wame Japanah, Siphiwe Phili Ereson, Abel Potani, Lenard Gola

Ku tiyeni kwa sunday kwapezeka, achinyamata aitana. Inu zabwino kumayamikira tabwerani sunday likubwerali masana...........
28/04/2026

Ku tiyeni kwa sunday kwapezeka, achinyamata aitana. Inu zabwino kumayamikira tabwerani sunday likubwerali masana.............tampangeni tag mzanu aone nawo izi💦💯💯💦💯💦💦

Ulendo osadziwa kathuUlendo oyenda ali chigonele Ulendo onyamulidwaUlendo ulowa mu tchalitchi cha Masintha komaliza osat...
26/04/2026

Ulendo osadziwa kathu
Ulendo oyenda ali chigonele
Ulendo onyamulidwa
Ulendo ulowa mu tchalitchi cha Masintha komaliza osati kudzapemphera kapena kudzayimba kwaya yawo ayi koma kudzatsanzika ndi anzawo.

Bambo B.B Chisale omwe anabadwa mu Chaka cha 1938 lelo analowa mu tchalitchi cha Masintha osati kukapemphera kapena kukayimba kwaya yawo yokondeka ya MADALA yomwe anayamba kuyimba mu chaka 1995 monga amachitila nthawi zonse koma kudzatsanzika ndi mpingo wa Masintha,abale ndi anzawo onse.

Iwo agwirapo ntchito zambiri zochuluka zapa mpingo monga kukhala nsungi chuma wa mpingo wa Masintha mu chaka cha 1991,akhalapo mlangizi ndi ma udindo ena.

Kunabwela anthu ochuluka kudzachitila umboni za imfa ya Mr B B Chisale omwe amwalira dzuro pa 25-04-2026 atagwa akuyimba nyimbo ku mapemphero a Chigwirizano cha abambo.

Nthupi la malemu komanso akulu a mpingo opuma Mr B B Chisale likhale likukalowa m'manda mawa pa 27-04-2026 ku Dedza Mayani.

Bambo B.B Chisale omwe malingana ndi akubanja komanso a chipatala nthenda yomwe yawatenga ndi shuga yomwe pa nthawi yi inali itatsika kwambri.

iwo asiya mkazi, ana 8 ndi zidzukulu 25.

Mzimu wawo uwuse mu mtendere.

OLEMBA - Emmanuel Mndala (Lilongwe, 26-04-2026)

25/04/2026

Tiyeni okondeka tizindikile kuti imfa timayenda nayo ndipo tikhale anthu osamala

Bambo B.B Chisale anadzuka bwino bwino lelo
Kukonzeka nthawi yabwino kupita ku Chigwirizano cha abambo
Pokhala munthu oyimba inafika nthawi kuti choir yawo iyimbe ya MADALA CHOIR
ali mkati moyimba iwowo nakhala oyambitsa yimboyo
Ali mkati moyimba anangogwa anzawo kumawona ngat mwina akupanga za sewero osadziwa kuti kunyamuka kunali komweko

Mulungu anatibisila manyamukidwe athu anthufe

PROGRAM YA MALIRO A MR B.B CHISALE

Maliro a akulu ampingo opuma aku Chisamba ward Bambo B.B Chisale akhala onyamula. Thupi lawo likaikidwa m'manda ku Mudzi kwawo ku Mayani m'boma la dedza.

Tsiku lonyamuka kupita ndi zovutazi ku Dedza ndi mawa.

Map- M'mbali mwa nsewu ochoka pa stage ya masintha kulowera ku matchansi opposite Zambezi Church.

Zikomo

Mzimu wawo uwuse mu mtendere

25/04/2026

Rest in peace Mr B.B Chisale ( first to the right) (oyamba kuchokela kumanja ) Madala choir Legend

MASINTHA CCAP will miss you 🙏🙏

Madongosolo onse tikhale tufotokoza posachedwa

25/04/2026

Big shout out to my newest top fans! Elube Mndala, Annie Mangeni, Clement Sandy, Bright Willian Phiri, Pritam Chakulamkamwa, Joseph Mchenga, John Ngwenya, Joseph Kacheche, Wetson Buwawa, Laston Phiri, Chifundo Chilima, Manuel Katengeza, Blessings Morgan Ganizani, Chisomo Phiri Kanyenda, Asante Edith Chikweza, Madalitso Amos, Elizabeth Kamphandira, Naomi Joshua, Rob Kay, Innocent Chikoti, Noel Frank Kambeu, John Moomba, Madalitso John, Nicodemo Kambiri Kambiri, Blessings Davie Mahhata, Maya Brand, Rose Ng'omba, Mayeso Banda, Florêncio Pires Tomussene, Chancy Herings Chikuni, Kambola Banda

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Masintha CCAP posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share