Nkhukwa Assemblies of God Youth Ministry

Nkhukwa Assemblies of God Youth Ministry Let us all rejoice in our Lord Jesus Christ.

12/06/2024

N R C!

05/07/2022

Chikondi cha Ambuye wathu chikhale ndi inu nonse ... Amen!

10/06/2022

Aroma 10 vs 9
Kuti ngati udzavomereza m'kamwa mwako Yesu ndiye Ambuye ndi kukhulupilira mu mtima mwako kuti Mulungu anamuukitsa kwa akufa, udzapulumuka.

10/06/2022

Masalmo 112
Haleluya. Wodala munthu wakuopa Yehova, Wakukondwera kwambiri ndi malamulo ache.
Mbeu yache idzakhala yamphamvu padziko la pansi

13/05/2022

Masalmo 37 ....Kusangalala kwa ochimwa kudzatha ndipo olungama adzakhalabe nathandizidwa ndi Mulungu..Usiku wabwino

11/05/2022

Loweruka tikuyenera kukakolora Chimanga kwa abusa... Tikakumane Ku church m'mawa

22/04/2022

We believe in Christ

Address

Mitundu Bunda
Lilongwe

Telephone

+265996505718

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nkhukwa Assemblies of God Youth Ministry posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share