MVAMA TV

MVAMA TV Mvama Television is a registered Tv under Nkhoma SYNOD situated in Area 49. The Minister is Reverend Hamilton Yasin Gammah

26/06/2026

Police Yanga

Sabata Lopatulika (Block Week) lero lafika pa tsiku lomaliza, ndipo wolalikira anali Abusa Alexander Kambiri pa mutu wak...
26/06/2026

Sabata Lopatulika (Block Week) lero lafika pa tsiku lomaliza, ndipo wolalikira anali Abusa Alexander Kambiri pa mutu wakuti: “Chiyero ndi Gwero la Kukula mu Chikhristu.”

Abusa Kambiri ati pali ena amene amadziwa Mawu a Mulungu koma amawagwiritsa ntchito pochita zinthu zoipa. Anenanso kuti ena amafotokoza bwino malemba, koma m’mitima mwawo mulibe choonadi.

Iwo ati Akhristu ayenera kukhala a chiyero mwa kukhala ndi moyo wogwirizana ndi zimene Mawu a Mulungu amanena.
A Kambiri apitiriza kunena kuti chimene chimapangitsa Akhristu kukhala ofooka pa nkhani za uzimu ndi kulephera kutsatira zimene amaphunzira m’Malemba.

Iwo alimbikitsa Akhristu kuti ataye makhalidwe oipa ndi kutsatira zimene Mawu a Mulungu amafuna.
Abusa Kambiri atinso kukhala Mkhristu wa chiyero kumatanthauza kukhala munthu wosunga mtima wabwino, wosasunga mangawa komanso wokhululuka anthu akamulakwira.

Pomaliza, Abusa Kambiri anathokoza Abusa Yassin Gama ndi mpingo wonse wa Mvama CCAP chifukwa chomupatsa mwayi wolalikira pa mapephero amadzulo a sabata ino. Anati akadzayitanidwanso mtsogolo, adzakhala wokondwa kubweranso.
Mwezi uno, Sabata Lopatulika lidayamba pa 22 June ndipo latha lero pa 26 June 2026.

Wolemba: Natasha Muthete

Ministry of Health and Sanitation, in partnership with UNICEF and the Government of Japan, has launched a one-year US$74...
26/06/2026

Ministry of Health and Sanitation, in partnership with UNICEF and the Government of Japan, has launched a one-year US$746,000 Integrated Emergency Health, Nutrition and WASH Response Project.

The project aims to provide essential health services in the vulnerable districts of Salima and Thyolo, which have been affected by child malnutrition, cholera outbreaks, and climate-related disasters.

Speaking during the launch, Principal Secretary for Administration Benston Chisamalile welcomed the initiative, saying the partnership will help improve access to critical health services for Malawi’s most vulnerable children and communities.

In his remarks, Japanese Ambassador to Malawi Naito Yasushi reaffirmed his government’s commitment to strengthening health systems and promoting innovations through partnerships the Malawi Government.

By Natasha Muthete

26/06/2026

BLOCK WEEK TEACHING (DAY 5)
PREACHER: REV. KAMBIRI
THEME: HOLINESS IS THE KEY TO SPIRITUAL MATURITY
TIME: 6:00PM-7:00PM

Lero pa 26 June 2026, ndi tsiku limene sukulu zambiri zinali kalikiliki kukonzekera m’mene ophunzira a  Form 4, adzakhal...
26/06/2026

Lero pa 26 June 2026, ndi tsiku limene sukulu zambiri zinali kalikiliki kukonzekera m’mene ophunzira a Form 4, adzakhalire ((Sitting Plan) polemba mayeso a MANEB sabata ya mawa.

Mayesowa adzayamba lolemba pa 29 June ,2026, mpaka pa 24 July 2026.

Ophunzira apa sukulu ya Secondary ya Mkomachi, Athens 3, komanso Dominion High school, akuyembekezeka kulembera mayesowa limodzi pa sukulu ya Mkomachi ku Area 49, mu mzinda wa Lilongwe.

Wachiwiri kwa mphuzitsi wamkulu pa sukulu ya Mkomachi a John Kaweta, ati iwo ngati sukulu ndi okonzeka bwino, ndipo apepha ophuzira kuti ayike chidwi chawo pa mayeso kuti achite bwino.
A Kaweta achenjeza olemba ndi olembetsa mayesowa kuti apewe m’chitidwe wachinyengo, chifukwa wopezeka akuphwanya malamulo adzaimbidwa mlandu.

Malinga ndi woyankhulira ku bungwe la MANEB, Angella Kash*tigu, ophuzira 197,502 (anyamata 102,981 ndi atsikana 94, 521) ndiwo akuyembekezeka kulemba mayesowa chaka chino

Wolemba: Maria Bosco

Competition and Fair Trading Commission (CFTC) has raised alarm over the continued sale of expired and potentially unsaf...
26/06/2026

Competition and Fair Trading Commission (CFTC) has raised alarm over the continued sale of expired and potentially unsafe goods across Malawi, urging consumers to be more vigilant when purchasing everyday products.

The warning comes after recent market inspections revealed a worrying number of expired items being sold in shops across several districts.

According to CFTC spokesperson Innocent Helema, the Commission conducted extensive inspections in Blantyre, Lilongwe, Mulanje, Salima, Nkhotakota and Chikwawa, where officers discovered a total of 891 expired products.

Helema said the findings reflect serious negligence by some traders and pose a direct threat to consumer safety if not urgently addressed.

He further said the inspection exercise uncovered a wide range of expired goods, including 101 dairy products, 112 packs of biscuits, 83 packs of noodles and cereals, 178 packets of chewing gum and mints, 172 chocolates and sweets, and 59 snacks and crisps.

In addition, 49 beverages, 38 sauce products and spices and 28 personal care and household items were also found to be past their expiry dates.

The exercise follows a similar operation conducted last week in Mangochi, Machinga, Zomba, Mzimba, Mzuzu and Kasungu, where 14 shops were found selling 649 expired and uncertified products.

By Chikondi Kuphata


Gift of the Givers Foundation has stepped in to support Malawians on voluntary repatriation from South Africa, providing...
26/06/2026

Gift of the Givers Foundation has stepped in to support Malawians on voluntary repatriation from South Africa, providing transport assistance amid growing demand for return journeys to Malawi.

With support from the organization, 8 buses have departed South Africa for Malawi (seven from Pietermaritzburg and one from Durban) with 11 more currently being processed.

The foundation's director Sheriffa Mia says they plan to sponsor up to 50 buses in total to help ease pressure on both the Malawian and South African governments, which have been coordinating the repatriation exercise.

The organization is also providing returns with basic supplies that include hygiene packs, snack packs, sandwiches, clean and safe water for drinking to sustain them along the way.

By Chikondi Kuphata


26/06/2026

NEWS REVIEW

The Department of Disaster Management Affairs (DoDMA) has moved the main reception and processing centre for Malawians r...
26/06/2026

The Department of Disaster Management Affairs (DoDMA) has moved the main reception and processing centre for Malawians returning from South Africa due to xenophobic attacks, from Kamuzu Stadium in Blantyre to Joyce Chitsulo Stadium in Mwanza.

According to DoDMA, the move is aimed at bringing services closer to the point of entry and improving the repatriation process. Returning citizens will now receive immigration clearance, registration, health screening and humanitarian assistance in Mwanza before travelling to their home districts.

The government has also deployed relief supplies and processing teams to Mwanza, while returnees will be provided with bus fare to reach their respective homes safely. Families are advised that all reception and processing activities will now take place in Mwanza.

By Gift Mfumuchaje

26/06/2026

MORNING MAGAZINE

Address

Area 49, Zebra
Lilongwe

Telephone

+265888862699

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MVAMA TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to MVAMA TV:

Share