WINN Soul's International Ministry

WINN Soul's International Ministry The fruit of righteous is a tree of life, and he who win souls is wise (proverb 11:30)

09/06/2023

May this weekend be your weekend that will end all your suffering and friction in the mighty name of Jesus Christ

26/04/2023

May the hand of God reach your needs im the name of Jesus Christ.

14/04/2023

Ngati ululu omwe ukudutsamo sukubweretsa mpindu kwa iwe, dziwa kuti mvuto ndi iweyo.

Yesaya 53:5

25/03/2023

Ndikuyitanira kwa Mulungu waku mwamba pa moyo wako tsiku la lero lisadathe ukhala utakumana ndi umboni wako mu dzina la Yesu khristu

16/03/2023

Ndikulengeza pa moyo wako madzulo ano mu dzina la Yesu khristu palibe waku banja lako afe nthawi yake isadakwane.

03/03/2023

Ndikumva mpokoso la umboni wako mwezi uno mu dzina la Yesu khristu. Landira umboni wako!!!

22/02/2023
22/02/2023

Mwezi uno usadathe ndikukuona Mulungu atakupanga kukhara mfulu ku matenda, matembelero akuthundu aja ndi kukuonongera zimu wa malire

19/02/2023

Nthawi zina umaona ngati satan wakupanikiza tsegula maso ako ngati Yobu ndi pomwe uzazindikire kuti Mulungu akumugwiritsa ntchito pokuchotsera kale lako kuti tsopano lako lifike osamataya mtima

15/02/2023

Banja siphikisano ayi kuti akakutchurani pa nzere kuti mwakhala number 1, koma kudekha ndi kudikira mofatsa umakumana ndi munthu oyenera ndi odziwa ntchito ya banja

15/02/2023

Address

A/24
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when WINN Soul's International Ministry posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to WINN Soul's International Ministry:

Share