Evangelical New Exodus Ministry

Evangelical New Exodus Ministry Our aim is to reach every part of the world with the gospel, as our heavenly father command us, In the book Of Mark 16:15

05/05/2023

VESI LATHU LALERO.

Mitambo 12:1-2

1Wokonda mwambo akonda kudziwa;

Koma wakuda cidzudzulo apulukira.

2Yehova akomera mtima munthu wabwino;

Koma munthu wa ziwembu amtsutsa,

05/05/2023

10Pomwepo abale anatumiza Paulo ndi Sila usiku kunka ku Bereya; pamene iwo anafika komweko analowa m'sunagoge wa Ayuda. 11Amenewa anali mfulu koposa a m'Tesalonika, popeza analandira mau ndi kufunitsa kwa mtima wonse, nasanthula m'malembo masiku onse, ngati zinthu zinali zotero. 12Ndipo ambiri a iwo anakhulupira; ndi akazi a Cihelene omveka, ndi amuna, osati owerengeka. 13Koma pamene Ayuda a ku Tesalonika anazindikira kuti mau a Mulungu analalikidwa ndi Paulo ku Bereyanso, anadza komwekonso, nautsa, nabvuta makamu. 14Pomwepo abale anaturutsa Paulo amuke kufikira kunyanja; koma Sila ndi Timoteo anakhalabe komweko.

14/09/2022

Genesis 1:22

And God bless them, saying, be fruitful, and multiply, and fill the water in the seas, and let flow multiply in the earth.

We play to God to bless every work of your hands today in Jesus Name

Amen

07/07/2022

M'NGONERO WA MAU

Yeremiya 31:3

Yehova anaonekera kwa ine kale, ndi kuti, Inde, Ndakonda iwe ndi chikondi cosatha; Cifukwa cace ndakukoka iwe ndikukukomera mtima.

Mulungu adatikonda ife ndi mtima wake onse mchifukwa chake adatikoka kuticosa ku Uchimo ndikutikomera mtima ndikutipulumutsa lilemekezeke dzina lake...

Tipemphere

Yehova mulemekezeke chifukwa cha chikondi chanu chosatha chomwe mwationetseranso ife ana anu tsiku la lero. Mwatisamala, mwatidyesa, mwatipewetsa ku zolusa zomwe zikadatenga moyo wathu.. mulemekezeke Yehova, pamene tikugona usiku uwu tikafuna kupezeka kwanu Yehova mukatiteteze Mudzina la Yesu Khristu. Halleluya

31/08/2021

Even When It Seems Like The End Of The Road, God Will Always Make A Way, Don't loose Hope And Just Keep On Praying♥️♥️♥️

27/08/2021

God Is Good

21/05/2021

Behold, the Lord hand is not shortened, that it cannot save; neither His ear heavy, that it cannot hear:
But your inequities have separated between you and your God, and your sin have bid his face from you, that he will not hear.

Isaiah 59:1-2

21/05/2021

Therefore by him let us continually offer the sacrifice of praise to God , that is the fruit of our lips , giving thanks to his name.
But do not forget to do good and to share, for with such sacrifices God is well pleased.

Hebrews 13:15-16

Address

Box 4 Area 18A
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Evangelical New Exodus Ministry posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Evangelical New Exodus Ministry:

Share