M'buka CCAP youth

M'buka CCAP youth Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from M'buka CCAP youth, Church, Area 36 , BOX 702, Lilongwe.

26/07/2026

Chimwemwe chimadza mmawa!!!!

Yambani tsiku lanu ndi kuchotsa mphepo lero.

Amzanu ayamba kale kuno 🔥🔥

Ife achinyamata a mpingo wa M'buka ndi Mwala  CCAP tili ndi ulendo wopita ku Dowa kukatumikira(Outreach). Mwa ichi week ...
24/07/2026

Ife achinyamata a mpingo wa M'buka ndi Mwala CCAP tili ndi ulendo wopita ku Dowa kukatumikira(Outreach). Mwa ichi week ino takhala tikupempha Mulungu mwa Kusala kudya kuti ateteze ndi kutsogola mu utumiki umenewu.

Lero, Friday 24th July 2026 madzulo ano, tili ndi night of prayer komwe tikhale tikupempha chifundo, zisomo pa utumiki wathu, chitetezo ngakhalenso kupereka mpingo wathu, dziko lonse mmanja mwa Mulungu.

Mapepherowa ayamba 8 koloko madzulo ano.

Malo: M'buka CCAP

Nonse muli oyitanidwa.

Zotsatira za fundraising yomwe idachitika Pa 13th July 2026.Mu mndime za magulu, Praise team ndiyomwe inathembetsa magul...
20/07/2026

Zotsatira za fundraising yomwe idachitika Pa 13th July 2026.

Mu mndime za magulu, Praise team ndiyomwe inathembetsa magulu onse, kuyipa pansi gulu la zisudzo, komanso media team.

Izi zikutanthauza kuti awa amayimba komanso kukonda Mulungu mwanjira yakupereka.

Ife tingoti Mulungu akulitse utumiki womwe adayikiza mwa Inu.

Zotsatira za fundraising yomwe idachitika Pa 13th July 2026.Dera la Mvunguti ndiwo adakhala akatswiri pa tsikuli. Derali...
20/07/2026

Zotsatira za fundraising yomwe idachitika Pa 13th July 2026.

Dera la Mvunguti ndiwo adakhala akatswiri pa tsikuli. Derali limapikisana ndi Madera monga Kachere, Station komanso Mchenga.

Ife tonse tikusangalala nawo pamodzi pamene akuchita molimbika ntchito yopereka chuma chotumikira nacho Mulungu.

Mulungu akudalitseni

12/07/2026
NoticeGood Afternoon!!!Malo asithidwa from Share World to SOS Primary SchoolTiyeni Nthawi.M'buka CCAP youth
06/07/2026

Notice

Good Afternoon!!!
Malo asithidwa from Share World to SOS Primary School

Tiyeni Nthawi.
M'buka CCAP youth

SPORTS DAYM'BUKA C.C.A.P VS MSOKHAMANJA C.C.A.PDate:6 July 2026Time:1:00pm up to 4:00pmLocation: SHARE WORLD @Games like...
04/07/2026

SPORTS DAY

M'BUKA C.C.A.P VS MSOKHAMANJA C.C.A.P
Date:6 July 2026
Time:1:00pm up to 4:00pm
Location: SHARE WORLD @
Games like football, Netball, Volleyball etc



Address

Area 36 , BOX 702
Lilongwe
207236

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when M'buka CCAP youth posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category