Jumbo Assemblies Of God Church

Jumbo Assemblies Of God Church Sharing God's words so that people receive salvation all over the world

06/06/2025

Mulungu amadzionetsera yekha

EKSODO 14:13-14
Mulungu anamuuza mose k*t awuze ana a Israel k*t aziyendabe chitsogolo asacheuke mbuyo

Ndimati ndikambe nanu abale wokondedwa k*t pamene tikukhala mmoyo wasautso tiyeni tisayang'ane mbuyo koma tipitebe chitsogolo pak*t mavuto tikudutsamo leroli simudzawawonaso ingakhale anthu atipeputse bwanj kaya k*tinyoza osadandaula kalikose pak*t Mulungu nthawi zonse amakhala pakati pathu

Limbani mtima, maso Anu penyani kwa Mulungu, Fuulirani kwa iye pak*t ndiko kuli mayankho a nyengo zanu

Read verse 3
02/07/2024

Read verse 3

22/05/2024

Nthawi ya chigumula Cha nowa Pali mbalame izi nkhwangwala ndi nkhunda.

Kodi pambalame ziwiri zimenezi zidachita chiyani? Ndipo ifeyo pa moyo uno tingaphunzirepo chani?
Amen

21/05/2024

Numeri 16:21 Tikuonapo nkhani yomwe Mulungu akumuuza Mose k*ti adzipatule pamahema a kola,Datan ndi abiramu.

Anthu atatu awa kola,Datan ndi abiramu anamuukira Mose ndipo anafuna k*ti atsogolere ana a Israel abwerere nawo ku dziko la Egypt koma Mulungu anakwiya nawo ndipo anamuuza Mose k*ti adzipatule pakati pawo.
Abale ndi alongo pamene tikukhala padziko lapasi Ili tikuyenera kumadzipatula pakati pa anthu amene akupanga zopandukira pamaso pa Mulungu chifukwa tikamakakamira Malo amenewa kudzapezeka k*t nafeso talowa nawo kagulu kameneko

21/05/2024

Mwadzuka bwanj kose komwe muli anthu okhulupirira pa dzina la yesu khristu. Dzina limene likaitanirapo timapezapo zinthu zochuluka monga:
1 mtendere
2 chikondi chokhazikika
3 chisomo
4 kukonderedwa
5 chitetezo pa moyo wathu
6 kuomboledwa

20/05/2024

Mukhale ndi usiku opambana Mulungu ak*tetezereni kwa oyipayo

20/05/2024

Funso la tsiku la lero

Kodi chiyero ndichani abale ndi alongo?

20/05/2024

Pali nyengo zina zikamabwera pa munthu Mulungu amafuna ationetsere k*t iye ndi ndani pamoyo wathu ndipo pakhoza kuchitika zinthu izi: 1 Mulungu k*tuma angel ake k*ti akhale thandizo monga adachita ndi Daniel mdzenje la mikango
2. Mulungu kuonekera yekha monga anachita ndi shadreck ndi abelenigo

Ndiye tisamataye mtima kose tikamakumana ndi mavuto chifukwa Mulungu wathu YESU khristu amakhala Ali pakati pathu ndipo ndiye thandizo la moyo wathu

18/05/2024

Masalimo 150:6 zakupuma zose zilemekeze Mulungu.

Abale wokondedwa mwa ambuye tikuyenera kumamulemekeza Mulungu pozindikira k*ti anatipatsa moyo wa ulere osati kumamulemekeza pamene tili pamtendere pokhapokha komaso pamene tikuyenda nyengo yamasautso ndipo tikatero yesu khristu mbuye wathu amachita zazikulu zomwe ife sitimaziyembekezera.

01/05/2024

Chomwe chikuvuta anthu masiku ano ndikusunga chiyelo koma baibulo limati odala iye Ali oyela mtima chifukwa adzaona Mulungu

Sharing God's words so that people receive salvation all over the world

31/03/2023

Mulungu wathu amasamala ndipo amateteza. Tiyeni tizimulemekeza iye

31/03/2023

John 3:16 For God so loved the world that He gave his only son that who so ever believe in Him should not perish but have everlasting life

Address

Kasungu
Lilongwe Area 15

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Jumbo Assemblies Of God Church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share