Jesus Christ spring of life

Jesus Christ spring of life OUR MANDATE IS TO BRING HOPE AND SALVATION

11/02/2026

TIKUPEMPHELERA ODWALA ONSE, MULANDILE MACHILITSO ANU LERO ,MU DZINA LA YESU KHRISTU.

04/02/2026

NTCHITO ILIYONSE YABWINO IMENE MULUNGU ANAYIYAMBA PA MOYO WANU, IPITILILE KUCHITIKA,MU DZINA LA YESU KHRISTU.

29/01/2026

Chilichonse chimene mukuyenera kukhala nacho January uno, chikufikeleni before 31. mu dzina la Yesu Khristu.

19/01/2026

Tikukupemphelerani kuti, dzanja la mphamvu la Mulungu lichotse chitonzo ndi manyazi pa moyo wanu, mu dzina la Yesu Khristu.

15/01/2026

Ambili mwayesera panokha ,koma zinthu sizikuyenda, ntchito mukugwila koma sizikusintha,ena mwayesela kukonda kaoma simukukondedwa,kupanga busness koma sizikuthekabe , Mukusowekela chisomo cha Mulungu pa moyo wanu, ndipo tikunenera landilani chisomo chakupitsa patsogolo mmoyo mwanu ,mu dzina la Yesu Khristu.

06/01/2026

Yohane 1 vs 16. Tikukupemphelerani kuti chaka chino cha 2026,Muyende mu chisomo cha Mulungu kufikila ku chisomo chochuluka ,mu dzina la Yesu Khristu.

03/01/2026

Lero Tikukupemphelerani kuti, Mulungu wakumwaba aphwanye satana aliyense ofuna kulimbana ndi moyo wanu chaka chino cha 2026 , mu dzina la Yesu Khristu. AROMA 16 VS 20.

22/12/2025

God will shut the mouth of your enemies

18/12/2025

Mulungu wakumwamba alowelelepo mu nyengo zako , mu dzina la Yesu Khristu.

14/12/2025

Kukoma ndi zifundo za YEHOVA zikulondoleni lero, mu dzina la Yesu Khristu.

12/12/2025

Tikupemphelera nonse amene mwakhala muku nyozedwa ,kutonzedwa ndi kusalidwa chifukwa cha mavuto,Mulungu achotse chitonzo ndi manyazi anu lero.ndipo Mulungu akuyalileni gome nkuona kwa adani anu,ndipo chikho cha madalitso anu chisefukile lero, mu dzina la Yesu Khristu.

Call now to connect with business.

11/12/2025

LERO TIKUKUPEMPHELERA IWE KUTI ,ZABWINO ZONSE ZIMENE MULUNGU ANAKUKONZELANI KUTI MUKHALE NAZO CHAKA CHINO CHA 2025 ZIKUFIKILENI PASANAFIKE PA 31. MU DZINA LA YESU KHRISTU.

Address

Likuni

Telephone

+265888028873

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Jesus Christ spring of life posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Jesus Christ spring of life:

Share