kachere SDA Church - Kasungu

kachere SDA Church - Kasungu Kachere SDA Church is located in Kasungu, central region of Malawi.

Linyangwa trip  achinyamata a AY kukatumikila
09/05/2026

Linyangwa trip achinyamata a AY kukatumikila

Happy Sabbath family 💐
08/05/2026

Happy Sabbath family 💐

"And let them make me a sanctuary; that I may dwell among them" Exodus 25:8Ngati chuma chathu sichitumikira Mulungu nde ...
29/04/2026

"And let them make me a sanctuary; that I may dwell among them" Exodus 25:8

Ngati chuma chathu sichitumikira Mulungu nde kuti chikutumikira Santana. Koma Yoswa akuti "Ndipo ngati kutumikira Yehova kukuipirani mudzisankhire lero amene mudzamtumikira, kapena milungu imene anaitumikira makolo anu okhala tsidya lija la mtsinje, kapena milungu ya Aamori amene mukhala m'dziko lao; koma ine, ndi a m'nyumba yanga, tidzatumikira Yehova" - Yoswa 24:15. Tiyeni ife tikhale oyamba kutumikira Mulungu limodzi ndi Nyumba yathu.

Tukuyitanirani la Sabata li ku Chilinganizo chomanga.

Ambuye akudalitseni

19/04/2026

Talembani zopemphererazo ku comment section. Tiyeni tizipemphererana wina ndi mzake

16/04/2026

*Kachere SDA Church*
*GVH Kambadza*
*TA Kachere na Pemba*
*Boma la Dedza*
*Malawi*

*Tsiku:* 15 April 2026

Mutu: *KUFUNA ACHIBALE A BANJA LA MPANDASONI*

*Moni kwa inu Amfumu*

Dzina langa ndine *Crynose Mpandasoni*, mwana wa *Fourpence Mpandasoni*. Ndikuchokera ku Zimbabwe. Ndinalemba kalatayi kuti ndipemphe chithandizo chanu pakufuna achibale anga.

*Bambo anga anabadwira kuno ku Dedza.* Dzina lawo ndi *FOURPENCE MPANDASON*. Anamwalira m’chaka cha 2003. Pa chiphaso chake cha Zimbabwe panalembedwa kuti anachokera ku: *Dedza, Kambadza na Pemba*.

Iye anachoka kuno m’chaka cha *1974* kupita ku Southern Rhodesia, tsopano Zimbabwe. Analinso ndi *m’bale wake dzina lake TIMOTHY MPANDASONI*. Onse anachokera kumudzi wa *Pemba*.

*Amayi a bambo anga* — agogo anga — ankatchedwa *aNadhungeya*. Bambo anga analinso ndi *mlongo wawo dzina lake aAlice*.

Tsopano popeza bambo anga palibenso, ine sindinakumaneko ndi achibale anga aku Malawi. Ndi chifuniro changa chachikulu kudziwa kwathu ndi kukumana ndi banja lathu ndisanafe.

*Choncho ndikupemphani modzichepetsa kuti mundithandize kufufuza:*
1. Ngati pali achibale a banja la *MPANDASON/Mpandasoni* m’mudzi wa Pemba kapena GVH Kambadza
2. Ngati alipo anthu okalamba amene amakumbukira *Fourpence ndi Timothy*, ana a *aNadhungeya*, amene anapita ku Zimbabwe mu 1974
3. Ngati alipo amene amadziwa *aAlice Mpandasoni*, mlongo wa bambo anga

*Zikomo kwambiri* chifukwa cha nthawi yanu ndi chithandizo chanu. Mulungu akudalitseni pa zonse.

*Wanu,*
Crynose Mpandasoni
*Nambala yanga ya foni:* +263 785 681 702
Calls and WhatsAp.

TIWADZIWE!!Full name: Bwanali Mphoka Date of birth: 7th April Professional: Lab Scientist Home village: Balaka, PhalulaK...
07/04/2026

TIWADZIWE!!

Full name: Bwanali Mphoka
Date of birth: 7th April
Professional: Lab Scientist
Home village: Balaka, Phalula
Kids: 1
Church position: Mkulu wa mpingo
Jesus way: Central
Ku AY: Master Guide
Favorite hymn: KMN 39
Favorite bible verse: Psalms 118:13
Favorite dish: Nsima ya mgaiwa served with boiled local chicken and beans

Join us to wish him a happy birthday in his new age
Bwanali Ofatsa Mphoka

KACHERE SDA CHURCH INDUCTS 132 YOUTHS INTO MINISTRY PROGRAMSKachere, Kasungu – March 28, 2026Kachere Seventh-day Adventi...
30/03/2026

KACHERE SDA CHURCH INDUCTS 132 YOUTHS INTO MINISTRY PROGRAMS

Kachere, Kasungu – March 28, 2026

Kachere Seventh-day Adventist Church in Kasungu successfully conducted an induction ceremony for its youth, with a total of 132 participants officially registered into various clubs of the Adventist youth ministry department

The event took place on the evening of March 28, the induction ceremony was coordinated by Master Guides Madalitso Sochera, John Mtenje, and Blessings Njolomole. Their leadership was instrumental in organizing the event and setting a strong foundation for youth activities in 2026.

The ceremony marked the beginning of active participation in the church’s youth clubs, including Adventurer, Pathfinder, and Senior Youth, all aimed at nurturing spiritual growth, leadership skills, and moral development among young people.

Speaking during the event, the organizers encouraged parents to actively support and allow their children to participate in Adventist Youth programs, highlighting their importance in shaping responsible, spiritually grounded individuals.

The event reflects the church’s continued commitment to empowering young people and strengthening youth ministry within the community.
Story by Nellie Gomani

Mkati mwa Sabata ya mapemphero a chinyamata
24/03/2026

Mkati mwa Sabata ya mapemphero a chinyamata

22/03/2026

Moyo wabwino! Thanzi la bwino! Uwu ndi moni omwe amapereka a gulu la za thanzi mu mpingo wa kachere, moni omwe Umatantha...
08/03/2026

Moyo wabwino! Thanzi la bwino!

Uwu ndi moni omwe amapereka a gulu la za thanzi mu mpingo wa kachere, moni omwe Umatanthauza kuti akhristu akakhala Wathanzi, mpingo onse umakhala Wathanzi..
Linali lasabata labwino pa 7 March 2026, tsiku lomwe depatiment ya health inasonkhanitsa mphamvu zawo kukatumikira ku Maranatha Branch ya kachere SDA church m’boma la kasungu mu chigawo cha Central Malawi conference (CMC)

Tsikuli linali lapamwamba kwambiri kwa mamembala aku Maranatha branch chifukwa anadalitsika mu uzimu komanso ku thupi chifukwa pambali pa ulaliki anapimidwa matupi awo ku matenda osiyanasiyana..

Tsikuli linayamba ndi sabata school yomwe inatsogoleleredwa ndi banja la a moyo omwe ndi akhristu a ku branch imeneyi
Kenako ulaliki omwe unalalikidwa ndi MG elder Bwanali Mphoka omwe unachoka mu buku la Habakkuk Makamaka pa chapter 2 vs 4, pomwe analimbikitsa mpingo waku Maranatha kukhala okula muchikhulupiliro.

Chigawo cha masana kunali kupima a khiristu komanso anthu ena, zokhudza thanzi lawo, mwa zina zomwe

This coming Sabbath 🔥You are all invited
08/01/2026

This coming Sabbath 🔥

You are all invited

Address

Kasungu
Kasungu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when kachere SDA Church - Kasungu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share