New Apostolic Church Kasungu West

New Apostolic Church Kasungu West New Apostolic church Kasungu West is a religious grouping . It is in Kasungu district,Malawi under Apostle Owen Kaira( Malawi Mzimba District)

*Uthenga wa malilo* Mwachison ndikulengenga za kumwalila kwa okondedwa Deacon chiyembekezo lisongwe wa pa mpingo wa mise...
08/07/2026

*Uthenga wa malilo*
Mwachison ndikulengenga za kumwalila kwa okondedwa Deacon chiyembekezo lisongwe wa pa mpingo wa misenza,koma anasamukila ku chidzenje,
Malingana ndi akubanja a priest Emanuel lisongwe Deacon chiyembekezo amwalila mmawa wa lelo pa 08/07/2026,
Dongosolo latsiku loyika ati uzabe akubanja akakhalilana pasi,
Uzimu wa Deacon chiyembekezo uwuse mu mtendele,
Zikomo
Ine Dr stonard madziayenda.

mtumwi Samson golar mwanzaanachititsa mapemphelo pa mpingo wa Chagumukile pa 19/04/2026 thawi ya 9:00.mapemphelo atatha ...
25/04/2026

mtumwi Samson golar mwanza
anachititsa mapemphelo pa mpingo wa Chagumukile pa 19/04/2026 thawi ya 9:00.
mapemphelo atatha kunali mwambo wopeleka mphatso ya mbuzi yomwe anapeleka ndi sister Esther zimba yemwe a abweletsa mpingowu ku delali mchaka Cha 1994.

Address

Box 168
Kasungu

Telephone

+265997313995

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when New Apostolic Church Kasungu West posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share