Lumbadzi Seventh day Adventist Church -

Lumbadzi Seventh day Adventist Church - Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Lumbadzi Seventh day Adventist Church -, Religious organisation, Dedza.

15/08/2026

Nyimbo yomwe mumaikonda!!

Lumbadzi Seventh-day Adventist Church

15/08/2026

DIVINE SERVICE

14/08/2026

Happy preparation day!!

LUMBADZI FUTURE AMO - KONDANA NAYE.

AMEN!

13/08/2026

Kodi mukudziwa kuti tikupezekelaso pa tsamba la mchezo la YouTube?

Link ili mu comment section kapangeni subscribe. 👇👇

AYAMBITSA GULU LA FUTURE ADVENTIST MEN PA MPINGO WA LUMBADZI SDA Pofuna kulimbikitsa udindo wa chi khristu pakati pa any...
12/08/2026

AYAMBITSA GULU LA FUTURE ADVENTIST MEN PA MPINGO WA LUMBADZI SDA

Pofuna kulimbikitsa udindo wa chi khristu pakati pa anyamata, mpingo wa Seventh-day Adventist ku Lumbadzi wayambitsa gulu la Future AMO.

Gululi lomwe cholinga chake ndi kufuna kulimbikitsa anyamata pa nkhani za uzimu cholinga chake nchakuti anyamata azitha kukumana kulimbikitsana wina ndi nzake kudzela mu kuimba komanso zina zambiri.

Poyankhula mmene amaitanila anyamata kuti alowe nawo gululi, yemwe akutsogolera gulu la Future AMO a Jones Million anati khomo lawo ndi lotsegula kwa mnyamata aliyense komanso abambo achichepele.

"Tayambitsa gulu ili kuti tizitha kukumana ngati anyamata kuuzana za Yesu komanso kulimbikitsana kudzera mu kuimba. Tikuitanila anyamata onse kuti tizikhalira limodzi," anatero a Million.

Future AMO imasonkhana lasabata lililonse nthawi ya masana pa nkhomaliro.

Jonathan Chauwa
Communications Department

Mwambo opeleka ma certificate kwa Amayi omwe amaliza maphunziro awo.Mpingo mukamva mukuti bwanji?
09/08/2026

Mwambo opeleka ma certificate kwa Amayi omwe amaliza maphunziro awo.

Mpingo mukamva mukuti bwanji?

21 WOMEN GRADUATE FROM 2026 DORCAS SEMINAR21 women at Lumbadzi Seventh-day Adventist Church have graduated from the 2026...
09/08/2026

21 WOMEN GRADUATE FROM 2026 DORCAS SEMINAR

21 women at Lumbadzi Seventh-day Adventist Church have graduated from the 2026 Dorcas Seminar, which was held from August 2 to 8 under the theme “Mayi wa Ngwiro,” led by Shepherdess Stella Kamgoma.

The week-long seminar focused on equipping women with spiritual, practical and physical skills to help them become a light in their homes, church and community.

Speaking during the service, Shepherdess Stella Kamgoma preached from Mark 9:14, encouraging the women to strengthen their faith and remain committed to God in their daily lives.

One of the graduates, Ellena Lungu described the seminar as fruitful, saying she had learned several practical skills, including baking, sewing and knitting, among others.

“The seminar was fruitful because I have learnt how to bake bread and how to knit. It was not only just that, I have also learnt how to do public speaking,” she said.

On Sabbath afternoon, the women had an opportunity to showcase the skills they acquired throughout the week. Following the programme, the women displayed their work and some of the food products were shared after the Sabbath.

The event shed light on the importance of empowering women with skills that can contribute to their spiritual growth, self-reliance and economic empowerment.

In her final remarks, Shepherdess Kamgoma said as Christians we need to be good people among each other today because what comes tomorrow it is only the creator that knows.

Writen by: Steve Mitole
Photos by: Jonathan Chauwa
Communications Department

SABATA LANU LINALI BWANJI??
08/08/2026

SABATA LANU LINALI BWANJI??

08/08/2026

AFTERNOON PROGRAM
DORCAS SEMINAR

08/08/2026

CLOSING OF DORCAS SEMINAR
DIVINE SERVICE
PREACHER: SHEPHERDESS KAMGOMA
MUSIC BY LUMBADZI DORCAS

Address

Dedza

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Lumbadzi Seventh day Adventist Church - posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share