Come To Jesus Choir Dedza Parish

Come To Jesus Choir Dedza Parish Choir things

05/01/2026
*_somewhere in 🔥🔥Salima
05/11/2025

*_somewhere in 🔥🔥Salima

Sometime back in Blantyre
18/05/2024

Sometime back in Blantyre

13/05/2024

TISAMAIWALE IZI AKATOLIKA ANZANGA MMAWA ULIWONSE

👇🏼👇🏼👇🏼👇🏼👇🏼



PEMPHERO LA M'MAWA.

Mulungu wanga, ndipereka kwa inu, ndi chithandizo cha Maria Woyera, zanga zonse , ntchito zonse ndidzazichita lero lomwe, ndi mafuno ndi maganizo anga onse.
Ndifunitsa kuchita kufuna kwanu kokha. Mundithandize kufikira nthawi yogona.

Amen 🙏



ATATE ATHU

Atate athu muli m'mwamba dzina lanu liyeretsedwe ufumu wanu udze, kufuna kwanu kuchitidwe , monga kumwamba choncho pansi pano.
Mutipatse ife lero chakudya chathu cha lero, mutikhululukire ife zochimwa zathu monga ifenso tikhululukira adani athu, musatisiye ife m'chinyengo, koma mutipulumutse ife kwa zoipa.

Amen 🙏



KUMVERA KWA APOSTOLI.

Ine ndimvera Mulungu Atate amphamvuzonse, amene adalenga dzilo lakumwamba ndi Dziko lapansi pino, ndipo Yesu Khristu , Mwana yekha, Ambuye athu amene adaikida m'mimba ndi Mzimu Woyera, nabadwa mwa Maria Virgo, adasauka kwa Ponsio Pilato, adampachika pamtanda adamwalira, adamuika m'manda, adatsikira kwa akufa, ndipo tsiku lachitatu lake adauka kwa akufa, adakwera Kumwamba, ndipo akukhala ku dzanja lamanja lA Mulungu Atate amphamvuzonse, adzafumira ko.weko kudzaweruka amoyo ndi akufa.
Ndimvera Mzimu Woyera, Eklezia Katolika Woyera, chiyanjano cha anthu oyera, chikhululukiro cha machimo, thupi lidzauka, ulipo moyo wosatha.

Amen. 🙏



TIKUONENI MARIA

Tikuoneni Maria wachaulere chodzaza, Ambuye ali nanu, ndinu wodala kopambana akazi onse, ndipo ngodalanso Mwana wanu Yesu.

Maria Woyera, Amai a Mulungu, mutipempherere ife ochimwa, tsopano ndiponso pa nthawi ya kufa kwathu.

Amen 🙏



KULAPA

Mulungu wanga, ndilapa, ndileka zakwaipa zanga zonse, chifukwa ndinu wabwino ndi wokondeka ndithu ndi wolanga anthu ochimwa.
Mundithandize ndi chaulere chanu kuti ndisachimwenso.

Amen 🙏



KUMVERA

Mulungu wanga ndimvera mau anu onse, monga *Eklezia Katolika* awamvera, nawaphunzitsa, ndimvera iwo chifukwa ndinu Mulungu woona ndipo *Eklezia* wanu sangathe

13/05/2024

TIYANKHULENI AMBUYE

13 MAY, 2024

LOLEMBA LA MULUNGU WA 7 WAPASAKA

MAU OYAMBA A MBUKU LA NTCHITO ZA ATUMWI 19:1-8

_Kodi mudalandira Mzimu Woyera pamene mudakhulupirira?_

Pamene Apolo adali ku Korinto, Paulo adayendera maiko apa mtunda, nakafika ku Efeso. Kumeneko adapezako ophunzira ena, ndipo adaŵafunsa kuti: “Kodi mudalandira Mzimu Woyera pamene mudakhulupirira?” Iwo adati: “Ndi kumva komwe sitidamve kuti kuli Mzimu Woyera.” Paulo adaŵafunsa kuti: “Nanga tsono mudabatizidwa ndi Ubatizo wotani?” Iwo adati: “Ndi Ubatizo wa Yohane.” Paulo adati: “Yohane ankabatiza anthu otembenuka mtima, ndipo iye yemwe ankauza anthuwo kuti akhulupirire wina amene adalikudza pambuyo pa iyeyo. Winayo ndiye Yesu.” Okhulupirira aja atamva zimenezi, adabatizidwa m’dzina la Ambuye Yesu. Pamene Paulo adaŵasanjika manja, Mzimu Woyera adadza pa iwo, ndipo adayamba kulankhula zilankhulo zosadziŵika, ndi kumalalika mawu ochokera kwa Mulungu. Anthuwo onse pamodzi adalipo ngati khumi ndi aŵiri. Paulo adaloŵa m’nyumba ya mapemphero ya Ayuda, ndipo pa miyezi itatu adakhala akulankhula molimba mtima. Ankakamba ndi anthu za Ufumu wa Mulungu, nayesa kuŵakopa.

Mau a Ambuye 🙏

NYIMBO YA SALIMO: SALIMO 68: 2-3AB, 4-5ACD, 6-7AB

Imbirani Mulungu nyimbo, inu maufumu apa dziko lapansi (33a).

Mulungu adzambatuke, adani ake amwazikane.
Onse amene amamuda, athaŵe pamaso pake.
Amwazeni iwowo monga m’mene mphepo imachitira utsi.
Anthu oipa aonongeke pamaso pa Mulungu,
Monga m’mene sera amasungunukira pa moto.

Imbirani Mulungu nyimbo, inu maufumu apa dziko lapansi.

Koma anthu anu Mulungu, akondwere, asangalale pamaso panu,
Inde, asekere ndi chimwemwe.
Muimbireni Mulungu, imbani nyimbo zotamanda dzina lake.
Kwezani nyimbo yotamanda Iye amene amayenda pa mitambo.
Dzina lake ndi Chauta, musangalale pamaso pake.

Imbirani Mulungu nyimbo, inu maufumu apa dziko lapansi.

Atate a ana amasiye ndiponso mtetezi wa amayi amasiye,
Ndi Mulungu amene amakhala m’malo ake oyera.
Anthu osiyidwa, Mulungu amaŵapatsa m

12/05/2024

✝️OSAMAIWALA IZI MADZULO ALIWONSE✝️

👇🏼👇🏼👇🏼👇🏼

✝️TIPEMPHERE✝️

Dzina la atate, ndi la mwana ndi la mzimu oyera. Amen

✝️PEMPHERO LA MADZURO ✝.

Mulungu wanga ndabweranso kwa inu madzuro ano ndi chithandizo cha Maria Woyera, ndikuthokozani chifukwa cha zabwino zonse zomwe mwandipatsa lero. Ndili ndi chisoni pokumbukira zoyipa zonse zomwe ndazichita lero, Koma ndikhulupilira chikhululukiro cha inu.

✝️ATATE ATHU ✝

Atate athu muli m'mwamba dzina lanu liyeretsedwe ufumu wanu udze, kufuna kwanu kuchitidwa, monga kumwamba choncho pansi pano.
Mutipatse ife lero chakudya chathu cha lero, mutikhululukire ife zochimwa zathu monga ifenso tikhululukira adani athu, musatisiye ife m'chinyengo, koma mutipulumutse ife kwa zoipa.

✝️TIKUONENI MARIA ✝

Tikuoneniaria wachaulele chodzadza Ambuye Ali nanu, ndinu wodala mwa akazi onse, ndipo ngodalanso mwana wanu Yesu. Maria woyera ,Amayi a Mulungu, mutipemphelere ife ochimwa, tsopano ndiponso pa nthawi akufa kwathu.

✝️MALAMULO A MULUNGU ✝

1. Usapembedze Mulungu wina koma ine ndekha

2. Usatchule pachabe dzina la Ambuye Mulungu wako.

3. Udzikumbukira kuyeretsa tsiku la Mulungu

4. Lemekeza Atate ako ndi amayi ako.

5. Usaphe
6. Usachite chigololo
7. Usabe
8. Usachite umboni wonama
9. Usasirire chikwati cha mwini
10. Usachite kaduka ndi zinthu za mwini.

✝️MLAMULO A EKLEZIA ✝

1. Udzafika ku Nsembe ya Misa pa tsiku la Mulungu.

2. Pa masiku omwewo mudzagwira ntchito.

3. Udzalandira sacrament la Kulapa chaka chili chonse

4. Udzalandira Ukaristia chaka chili chonse pa nthawi ya Pasaka.

5. Udzapunguza ndi kusala nyama pa masiku awiriwa: tsiku la phulusa ndi tsiku Lachisanu loyera.

6. Udzapereka mtulo chaka chili chonse.

✝️KUMVERA ✝

Mulungu wanga ndimvera Mau Anu onse monga Eklezia katolika awamvera nawaphunzisa ndiwamvera

Ndiwamvera Iwo chifukwa ndinu Mulungu woona ndipo Eklezia wanu sangathe kulakwa Amen

✝️KUKHULUPILIRA ✝

Mulungu wanga, ndikhulupilira chaulere chanu pansi pano ndi moyo wosatha kumwamba, chif

12/05/2024

CATHOLIC DAILY MASS READINGS

MAY 12, 2024

SOLEMNITY OF THE ASCENSION OF THE LORD

LECTIONARY 58

First Reading
Acts 1:1-11

In the first book, Theophilus, I dealt with all that Jesus did and taught until the day he was taken up, after giving instructions through the Holy Spirit to the apostles whom he had chosen. He presented himself alive to them by many proofs after he had suffered, appearing to them during forty days and speaking about the kingdom of God. While meeting with them, he enjoined them not to depart from Jerusalem, but to wait for “the promise of the Father about which you have heard me speak; for John baptized with water, but in a few days you will be baptized with the Holy Spirit.” When they had gathered together they asked him, "Lord, are you at this time going to restore the kingdom to Israel?" He answered them, “It is not for you to know the times or seasons that the Father has established by his own authority. But you will receive power when the Holy Spirit comes upon you, and you will be my witnesses in Jerusalem, throughout Judea and Samaria, and to the ends of the earth.”When he had said this, as they were looking on, he was lifted up, and a cloud took him from their sight. While they were looking intently at the sky as he was going, suddenly two men dressed in white garments stood beside them. They said, “Men of Galilee, why are you standing there looking at the sky? This Jesus who has been taken up from you into heaven will return in the same way as you have seen him going into heaven.”

The word of the Lord 🙏

Responsorial Psalm
Psalm 47:2-3, 6-7, 8-9

R. (6) God mounts his throne to shouts of joy: a blare of trumpets for the Lord.
or: R. Alleluia.

All you peoples, clap your hands, shout to God with cries of gladness, For the LORD, the Most High, the awesome, is the great king over all the earth.

R. God mounts his throne to shouts of joy: a blare of trumpets for the Lord.
or: R. Alleluia.

God mounts his throne amid shouts of joy; t

21/03/2024

Good morning members here

11/09/2022

Come to Jesus live on stage

Address

Dedza

Telephone

+265992908494

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Come To Jesus Choir Dedza Parish posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Come To Jesus Choir Dedza Parish:

Share