Chiradzulu Christ Ambassadors Ministry

Chiradzulu Christ Ambassadors Ministry Youth Ministry( utumiki wachinyamata) Okweza ndikufalitsa Khristu Yesu. Mateyu 28:19

08/04/2026

Don't wait someone to remind you that the mission of serving lives is not yet over. Preach the gospel everywhere. Have a blessed night

25/12/2024

Happy Christmas

20/07/2024

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Michael Saka, Chikondi Chatha, Nana Akhimad, Tamala Mchiswe

08/07/2024

May God of host extend your territory this month of July

16/08/2023

How many of us have managed to attend the anannual convention?

06/06/2023

Kugona mkosavuta kukada koma kuti tidzuke zimatengera wa ku mwamba atidzutse. Alemekezeke mulungu wa moyo

10/02/2023

Musanyedwe Mulungu sanyozeka, Chimene munthu achifesa chimenenso azatuta. Agalatiya 6:7

02/01/2023

Alemekezeke Mulungu watisamalira komanso kutisunga ndi moyo chaka cha 2022. Pomwe tayambanso chaka cha 2023 timupemphe ayende nafe. Mukhale ndi chaka chatsopano chopambana.

24/08/2022
24/08/2022

Android Holy Bible, King James Version

21/08/2022

Mwadzuka bwanji abale ndi alongo konse komwe muli? Verse lathu la lero likuchokera pa Masalimo 119 vs 11. Tiyeni tiwerenge ndithu. Ambuye akudaliseni

Address

Chiradzulu Road
Chiradzulu

Telephone

+265884002831

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chiradzulu Christ Ambassadors Ministry posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share