Akhristu olimba mchikhulupiliro

Akhristu olimba mchikhulupiliro Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Akhristu olimba mchikhulupiliro, Religious organisation, jowkim chisano Road, Blantyre.

03/02/2026

Zosatheka ndi munthu zitheka ndi Ambuye.
Usataye mtima pempherabe

02/02/2026

MADZULO ANO TIYENI TIMVETSE BWINO KUTUMA KWA AMBUYE YESU

Mateyu 10
9Musadzitengere ndalama zagolidi, kapena zasiliva, kapena zakobiri m'malamba mwanu; 10kapena thumba la kamba la kunjira, kapena malaya awiri, kapena nsapato, kapena ndodo; pakuti wanchito ayenera kulandira zakudya zace.

Pamene tawerenga Luka 22

35Ndipo anati kwa iwo, Pamene ndinakutumizani opanda thumba la ndalama, ndi thumba la kamba, ndi nsapato, munasowa kanthu kodi? Anati iwo, Iai. 36Ndipo anati kwaiwo, Koma tsopano, iye amene ali ndi thumba la ndalama, alitenge, ndi thumba la kamba lomwe; ndipo amene alibe, agulitse copfunda cace, nagule lupanga,

KODI MAU A TESU KHRISTU AKUTIPHUNZITSA CHIYANI POMVETSERA MAVERSE AWIRI AMENEWA?

Address

Jowkim Chisano Road
Blantyre

Telephone

+265881248982

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Akhristu olimba mchikhulupiliro posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share