M'bawa SDA Future Adventist Men - M'ba FAM

M'bawa  SDA Future Adventist Men - M'ba FAM Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from M'bawa SDA Future Adventist Men - M'ba FAM, Religious organisation, Blantyre.

Mwadzuka bwanji mipesa ndi ena tonse pamudzi panoLelo pa 29 May 2026 nkukhalanso tsiku lokonzekela maola asabata tafuna ...
29/05/2026

Mwadzuka bwanji mipesa ndi ena tonse pamudzi pano

Lelo pa 29 May 2026 nkukhalanso tsiku lokonzekela maola asabata tafuna kuyamikila komanso kuthokoza KUZIPELEKA, LUSO, KUZICHEPESA komanso MALANGIZO amunthu wamkuluyi .kupezeka pakati pathu sitimachitenga chinthu chopepuka koma m'dalitso okhaokha.

Ifetu mowanyadila timawatchula dzina lawo ndipo nawonso zimawasangalasa SYL VASCO PAFUPI amenenso ali adventurer director wa ZONE komanso district coordinator wa Michiru district .

DOLO KWAMBIRI
MULANDILE ULEMU KUCHOKA KWA ANYAMATA A M'BA FAM.

Mwaswela bwanji agulu Dzulo pa 23 May 2026 mbiri yalembedwa pamene M'bawa fam imakhazikisidwa pa church,  ndipo chochiti...
24/05/2026

Mwaswela bwanji agulu

Dzulo pa 23 May 2026 mbiri yalembedwa pamene M'bawa fam imakhazikisidwa pa church, ndipo chochitikachi chinaphatikizana ndi fundraising komanso kutulusa nyimbo zomvela zili zomwe ndi LAPA komanso ADAM . Posachedwapa tikhale tikufotokoza mene mungazipezele nyimbo zimenezi kuti nanu mudalitsike nawo.

mukhale ndi tsiku lopambana.

22/05/2026

Mwadzuka bwanji mipesa ndi ena tonse pamudzi pano
Tsiku takhala tikudikila lija ndimawa pamene M'bawa young amo ili ndi group launch komanso fundraising mawamawali zonsetu zikhale zichitikila ku M'bawa sda church.

Koma zonsezi ziyambika lelo ndikusegulila sabata .

nonse ndinu olandilidwa!!!!!!!

07/05/2026

With Ndirande Central Future Adventist Men – I just got recognized as one of their top fans!

Mwaswela bwanji anthu a Mulungulasabata likubwelali kopita nde kulipo kale  tonse tukakumana ku M'bawa  sda church pamen...
07/05/2026

Mwaswela bwanji anthu a Mulungu

lasabata likubwelali kopita nde kulipo kale tonse tukakumana ku M'bawa sda church pamene atsikana a young Dorcas alindi chochitika patsikuli

kupezeka kwanu kuzakhala m'dalitso koposa
i will go

Hope we are all fine hereHappy sabbath allWe are counting down five weeks remaining M'bawa young amo
18/04/2026

Hope we are all fine here
Happy sabbath all

We are counting down five weeks remaining
M'bawa young amo

Morning  good people This is the  time we have been waiting for,  M'bawa amo is having group launch and fundraising on 2...
11/04/2026

Morning good people

This is the time we have been waiting for, M'bawa amo is having group launch and fundraising on 23 May 2026 let's all get prepared and come in numbers 😇😍.

Happy sabbath to you all
Stay blessed

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when M'bawa SDA Future Adventist Men - M'ba FAM posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share