07/02/2026
🔞+
Zinthu zimene zimachitika pakati pa okwatirana kuti asangalatsane, zokhazo zimene sizinalumphe malire a Sharia, n’zololedwa.
1: 🍑
Ngati mzimayi wasankha kuti akhale ndima 11, ndicholinga chofuna kumusangalatsa mamuna wake,izi ndizololedwa ngati mmene akuloledwanso kuboola mapikaniro ndikuikamo ndolo kuti azikongoletse kwa mamuna wake...
Penanso mzimayi akabeleka lake Malawi yake imatha kukhala yaikulu moti mamuna wake amangosambira, mzimayi akuloledwa kutenga mankhwala kuti lake Malawi yake ibwerere kuti mamuna wake adzisangalala bola zisawononge ndata komanso Gadafi, zisayambitse matenda, ndipo zisakhale zoopsa.
Choncho mu izi palibe kusintha chilengedwe cha Allah, Principle pa zinthu zomwe sisizili mgulu la ibada imati:
الأصل في الأشياء الإباحة
“Chinthu chilichonse tsinde lake, chimakhala chololedwa mpaka patabwera umboni kuti ndi choletsedwa.”
2. 🍆
Mankhwala okulitsa Gadaf ali ololedwa pamene mamuna akuona kuti mthinko wake ndiwaung,oni moti sukufikila pansi pa photo, kotero mkazi wake akumadandaula kuti mthinko ukuchepela mkaba, heavy kwambiri, basi palibe vuto kuti amwe mankhwala opereka thanzi kuti mthinko ukhale size yabho monga anthu ena, osati kuchikulitsa chili chachikulu kale kufuna kulanga mkazi wa Ndata yopheeketsa ayi... koma ngati ka mthikoko kachepa ndipo mankhwala ukufunawo alibe chiopsezo choti amayambitsa matenda, kupweteka, kapena kuwonongeka chida... basi achikulitse ndithu kuti banja lawo likhale losangalatsana.
Pokhapokha ngati mankhwalawo ali ndi zoopsa(ma side effects),
kapena amayambitsa matenda, kupweteka, kapena kuwonongeka,
pamenepo zimakhala zoletsedwa, chifukwa:
لا ضرر ولا ضرار
“Musapase vuto wina, ndipo musalole kupasidwa vuto".
Wamva bwanawe...?
: AI
DEEN TALK SHOW