United Pentecostal Church of Malawi

United Pentecostal Church of Malawi Welcome to the official page of the United Pentecostal Church Malawi.

Mwaswera?Si bas apa tikakumana pa 28 August 2026?Mention or tag anzanu amene simukufuna ajombe ku General Conference!
17/08/2026

Mwaswera?
Si bas apa tikakumana pa 28 August 2026?

Mention or tag anzanu amene simukufuna ajombe ku General Conference!

15/08/2026

Good morning
Teaching by Bishop Kanyema ( Lilongwe District presbyter )

🔥🔥🔥🔥🔥🔥 Tamvetseni

Zomba on fire🔥🔥🔥🔥Tiyeni kuzomba week ino  Tiyen tiyeni tiyeni tiyeni!
13/08/2026

Zomba on fire🔥🔥🔥🔥
Tiyeni kuzomba week ino



Tiyen tiyeni tiyeni tiyeni!

12/08/2026


Teaching by Bro A Mang’ando from Lilongwe.

Timvetsere kenako tiphunzire kenako tikachite🔥

09/08/2026

How was your Sunday?

Mzuzu UPC
teaching by Mr Ng’ambi

Be blessed 😇

Kodi inu mbiri ya ma General conferences mukuyidziwa? Tiuzeni kuti ichi chinali chaka chanji? Atakhonzeyo timuthokoza nd...
08/08/2026

Kodi inu mbiri ya ma General conferences mukuyidziwa?
Tiuzeni kuti ichi chinali chaka chanji? Atakhonzeyo timuthokoza ndi buku la nyimbo ( oyambirirayo )

Share church old pictures. 0881546541
Mwadzuka bwanji?

inali konko

Good morning Saints !!!!!Mwadziwapo ndani apa?After 2years Bible School on the last day 🔥🔥🔥🔥  inali konkoNgati muli ndi ...
07/08/2026

Good morning Saints !!!!!
Mwadziwapo ndani apa?
After 2years Bible School on the last day 🔥🔥🔥🔥
inali konko

Ngati muli ndi zinthuzi zakale za mpingo
Share #0881546541 ( whatsapp )

 ?Apostolic Life Centre 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥Mwadzuka bwanji?
05/08/2026

?
Apostolic Life Centre 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Mwadzuka bwanji?

Kopita musankha nokha weekend iyiKoma week ino zochita nzambiri 🔥🔥🔥🔥🔥 Zomba Mangochi Chiladzulu Inu mupita kuti inu?
30/07/2026

Kopita musankha nokha weekend iyi
Koma week ino zochita nzambiri
🔥🔥🔥🔥🔥
Zomba
Mangochi
Chiladzulu

Inu mupita kuti inu?

27/07/2026


MwaYesu mwaYesu mwaYesu …………………….
Tiuzeni nyimbo mmayikonda ija mwina tikayimbe ku general conference

Address

CC 941, Kasungu Crescent RD
Blantyre
312225

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when United Pentecostal Church of Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share