Pastor Vincent Mtira

Pastor Vincent Mtira Senior Pastor at Glory to God Ministries (GGM), an interdenominational Ministry, devoted to nurturing souls and building a people grounded in faith and love.

22/08/2026

SATURDAY SERVICE WITH PASTOR VINCENT MTIRA | WISDOM SERIES

22/08/2026

SATURDAY SERVICE WITH PASTOR VINCENT MTIRA | WISDOM SERIES | 22 AUG 2026

❗COME AND RECEIVE YOUR BREAKTHROUGH❗‎‎Loweluka lino tilindi Service yapadela yomwe ndidzafotokoze bwino m'mene Inu munga...
21/08/2026

❗COME AND RECEIVE YOUR BREAKTHROUGH❗

‎Loweluka lino tilindi Service yapadela yomwe ndidzafotokoze bwino m'mene Inu mungagwilitsire ntchito Nzeru, Chidziwitso komaso Kumvesesa kuti muchite bwino mumagawo onse a Moyo wanu.

‎Service imeneyi odwala azalandira machiritso ndipo omangidwa mumagawo osiyanasiyana adzamasulidwa, Ndizakupemphererani Inu ndi apa Banja panu ndipo kudzodza kuzayenda pa nyengo zanu.

‎Bwelani muzalandire kubowoleza kwanu.

‎🕢 SERVICE STARTS AT 9:30AM SHARP
‎📅 KANJEDZA PRIMARY SCHOOL HALL

‎Itanani abale ndi anasi ndipo bwerani, ambuye wakonzeka kuyendera nyengo zanu magawo onse. 🙏

HAPPY BIRTHDAY, MAI BUSA RASHEENA MTIRA 🎂 🍰 🎂 ‎We have a huge celebration in the house! Today is the birthday of our bel...
20/08/2026

HAPPY BIRTHDAY, MAI BUSA RASHEENA MTIRA 🎂 🍰 🎂

‎We have a huge celebration in the house! Today is the birthday of our beloved Mai Busa Mtira, a very loving and caring woman.

‎What a blessed day it is for the house of GGM! Truly, we love and celebrate you, Mama, You are a blessing to many. 🥳🥳🥳🥳🥳🥳

LINGALIRO LA LERO📌-Ndi Pastor Vincent MtiraMiyambo 24:3 📖 Nyumba imamangidwa ndi nzeru, ndipo imakhazikika ndi anthu odz...
19/08/2026

LINGALIRO LA LERO📌
-Ndi Pastor Vincent Mtira

Miyambo 24:3 📖
Nyumba imamangidwa ndi nzeru, ndipo imakhazikika ndi anthu odziwa zinthu;

PEMPHERO: 🙏
Atate ndipatseni Nzeru zopangira zinthu zikulu zikulu komanso zogwirika, mudzina la Yesu khristu.

Zichitike pa Moyo wanu monga mwapempherera. Tiyeni tikhale pa mawu awa lero.

15/08/2026
"Mawu a Mulungu akhale Ulamuliro otsiliza pa moyo wanu"Pamene kalikonse kakuyankhula lolani kuti chomwe mawu a Mulungu a...
11/08/2026

"Mawu a Mulungu akhale Ulamuliro otsiliza pa moyo wanu"

Pamene kalikonse kakuyankhula lolani kuti chomwe mawu a Mulungu akunena pa nyengo yanuyo chikhale chotsiliza. Liwu la Yehovah silibwelera chabe. The word of God works 🙏

Ndikukulimbikitsani kuti mupeze mpata ndikuwoneranso kachikena teaching ya Loweluka lathali.

08/08/2026

SATURDAY SERVICE WITH PASTOR VINCENT MTIRA | HOW TO MAKE THE WORD OF GOD WORK

Address

Blantyre

Telephone

+265888752503

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pastor Vincent Mtira posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Pastor Vincent Mtira:

Shortcuts

Share