Ps. Stanley J. Zimenyana

Ps. Stanley J. Zimenyana Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Ps. Stanley J. Zimenyana, Christian church, Blantyre-kabula, Blantyre.

Civumbutso 19 v 10 Pakuti umboni ya Yesu christ ndi mzimu "wakunenera"mawu oti "kunenera" mukunena kwina ndikoti "kuchit...
22/08/2024

Civumbutso 19 v 10
Pakuti umboni ya Yesu christ ndi mzimu "wakunenera"

mawu oti "kunenera" mukunena kwina ndikoti "kuchitira umboni",mvesera mulungu(YEHOVAH) akachita zinthu pa moyo wako,iwe mwini ndikumati ambuye ndapambana bwanji ineyo kuti munditere,amakhakuti akukupanga iwe kukhala mboni yodalirika ya uthenga wabwino kwa anthu onse

Iye ndimmene aliri ndiye YEHOVAH
17/08/2024

Iye ndimmene aliri ndiye YEHOVAH

This version of Facebook uses less data and works in all network conditions.

Kupempherera tsogolo(Destiny) ndikofunika kwambiri kaamba kokuti munthu kuti ukhale muchimene mulungu(Yehovah),anakulemb...
17/08/2024

Kupempherera tsogolo(Destiny) ndikofunika kwambiri kaamba kokuti munthu kuti ukhale muchimene
mulungu(Yehovah),anakulembera kuti uzakhala kumakupanga kukhala muchimenecho mwachangu

is God's character

Dalitso lamulungu(Yehovah) liri pa mutu pako nthawi zonse
17/08/2024

Dalitso lamulungu(Yehovah) liri pa mutu pako nthawi zonse

Address

Blantyre-kabula
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ps. Stanley J. Zimenyana posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share