26/07/2026
KUOPSA KOONERERA MAPORNOGRAPHY ( ZOLAURA)⚠️⚠️⚠️
🔴 Zolaula kapena mapor nography
👉Ndi mabuku, zithunzi, mavidiyo,,,,,,etc omwe amafotokoza kapena kuonetsa anthu osavala (aumaliseche) ndi mchitidwe wogonana pofuna kumpanga munthu kuti akopeke ndi zinthuzo ndikuti zilakolako zake zikathe kukulitsidwa.
👉 Mavidiyo ndi zinthuzi zambiri zolaura zimapangidwa ndi akumidima pofuna kugwetsa ndi kuononga akhristu komanso miyoyo yochuluka . Anthu ambiri akukathera kumoto(Hell) chifukwa Cha kuonera zolaura( mapornography)
👉Ma internet page monga ###, XNXX , XVIDIOS, WAPTRICK,,,,,ndi ena otero onsewa anapangidwa ndi akumidima ndipo akupanga zithunzi, Mavidiyo ndi zinthu Zina zolaura ngati chida chimodzi champhamvu chogonjetsera akhristu ochuluka.
^_^ Palnso ena omwe amajambula ena amalemba zolaura KOMA iwo sakudziwa kuti ali m'bugwe la satana ndipo satana akuwagwiritsa ntchito.
👂M'zolaura muli chiwanda champhamvu chomwe chimatchedwa kuti *ma********on spirit* chiwandachi chikakhala mwa munthu chimampanga munthu kuti azibunyula (ma******te) . Ukundiko kuseweretsa mariseche.
😭😭😭 Anthu ambiri lero akumaseweretsa maliseche, indedi akhristu ochuluka lero akumaseweretsa maliseche 😭😭😭
😮Kodi kuseweretsa mariseche ndikutani??
•pali mafotokozedwe ambiri monga m'nyamata ndikufotokoza ; kuseweretsa mariseche ndiko kutaya mas***m (umuna)
😭😭😭
•umakhala kuti uli ndichilakolako Cha Mphamvu chofuna kupanga chigololo, ndiye basi umayamba kutaya ma s***m pansi, limene lilitchimo, m***a kuwerenga (📖Geneses 38:8-10) pakupezeka nkhani inayake ya ana awiri a Yuda , Mwana woyamba anali Eli wachiwiri anali Onani, Ndiyeno Eli anafa nasiya Mkazi ndipo Yuda anauza Onani kuti tenga Mkazi wa M'bale wako um'balire ana M'bale wako , kuti dzina lake lake lisafafanizidwe mu Israeli. Ndipo Onani panthawi yomwe anali kugona ndi Mkazi wa M'bale wake anali kutaya pansi mas***m(umuna) kapena mbeu, kuti Mkazi uja asakhale ndi mwana , ndipo mapeto ake Mulungu anamupha Onani.