Makande turn off Living waters church

Makande turn off Living waters church GOD IS #1

01/01/2024

IN 2024 God is going to be on your side, just believe.

31/12/2023

2024 The year of heavenly vision

23/06/2023

NKHANI YOMVETSA CHISONI, IFE NGATI MAKANDE TURN-OFF TILI OKHUDZIDWA NDI IMFA YA CHIWALO CHATHU SHAROM YEMWE WATISIYA LERO PA 23,JUNE 2023, MALIRO NDI OYIKA MAWA PA 24/6/23. AKUBANJA TILI NANU LIMODZI PA NTHAWI YOWAWITSAYI, TIKAMALIRA TIDZINGOYANG'ANA PA MTANDA WA KHRISTU YESU.

19/06/2023

Cenjezo lakuti afune Nzeru nalewe njira za oipa.
miyambo 4:1-2

1Ananu, mverani mwambo wa atate,

Nimuchere makutu mukadziwe luntha;

2Pakuti ndikuphunzitsani zabwino;

Musasiye cilangizo canga

CHILANGIZO CHA YEHOVA TIMACHIPEZA MUBAIBULO TIYENI TIDZILIWELENGA NTHAWI NDI NTHAWI KUTI TIKONZE NJIRA ZATHU,,, AMEN!!!

17/06/2023

WE R LIVING WATERS AND WE R VERY PROUD TO BE called ANA A APOSTLE NDOVIE

28/01/2023

MAWA LAMULUNGU TIPITE KU CHURCH MWACHANGU, KOMANSO ONSE OMWE TIKUSALA KUDYA TIKUFUNSIDWA KUPITA KU CHURCH MMAMAWA ZEDI 7 o'clock

GOD IS DOING ALOT TO YOU AND ME!!!Let's give him praises and honor
16/10/2021

GOD IS DOING ALOT TO YOU AND ME!!!
Let's give him praises and honor

28/08/2021

When coming to church plz don't forget to bring your bibles

28/08/2021

TOMORROW IS SUNDAY GET READY TO BE BLESSED

02/02/2021

Hallelujah

Address

Chiradzuru
Blantyre

Telephone

+265995500623

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Makande turn off Living waters church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Makande turn off Living waters church:

Share