Bible Society of Malawi

Bible Society of Malawi God's Word, Life for All. Mau a Mulungu Ndiwo Moyo Kwa Onse.
(1)

25/08/2026
Munthu wokhumba moyo ndani, wokonda masiku, kuti aone zabwino? Uletse lilime lako lisatchule zoipa, ndipo milomo yako is...
20/08/2026

Munthu wokhumba moyo ndani, wokonda masiku, kuti aone zabwino? Uletse lilime lako lisatchule zoipa, ndipo milomo yako isalankhule chinyengo. Futuka pazoipa, nuchite zabwino, funa mtendere ndi kuulondola. Masalimo 34:12-13

Yembekeza Yehova, nusunge njira yake, ndipo Iye adzakukweza kuti ulandire dziko. Pakudulidwa oipa udzapenya. Masalimo 37...
17/08/2026

Yembekeza Yehova, nusunge njira yake, ndipo Iye adzakukweza kuti ulandire dziko. Pakudulidwa oipa udzapenya. Masalimo 37:34

Mumtima mwake munthu wopusa amati,“Kulibe Mulungu.”Anthu otereŵa ndi oipa,amachita zonyansa,palibe ndi mmodzi yemwe woch...
16/08/2026

Mumtima mwake munthu wopusa amati,
“Kulibe Mulungu.”
Anthu otereŵa ndi oipa,
amachita zonyansa,
palibe ndi mmodzi yemwe wochita zabwino. Masalimo 52:1

MudzanditsitsimutsansoInu amene mwandiwonetsa mavuto ambiri oŵaŵa,mudzanditulutsanso m'dzenje lozama la pansi pa nthaka....
15/08/2026

Mudzanditsitsimutsanso
Inu amene mwandiwonetsa mavuto ambiri oŵaŵa,
mudzanditulutsanso m'dzenje lozama la pansi pa nthaka. Masalimo 71:20

Ngakhale munthu akhale wolemera chotani,komabe akasoŵa nzeru,adzafa chabe ngati nyama zakuthengo.Masalimo 49:20
13/08/2026

Ngakhale munthu akhale wolemera chotani,
komabe akasoŵa nzeru,
adzafa chabe ngati nyama zakuthengo.
Masalimo 49:20

Musadalire kulanda mwachinyengo, kapena katundu wobedwa; ngakhale chuma chanu chichuluke, musayike mtima wanu pa icho.Ma...
12/08/2026

Musadalire kulanda mwachinyengo, kapena katundu wobedwa; ngakhale chuma chanu chichuluke, musayike mtima wanu pa icho.
Masalimo 62:10

Carry God's Word wherever you go!We are excited to present to you all "Bible Langa," the essential app for reading and l...
11/08/2026

Carry God's Word wherever you go!

We are excited to present to you all "Bible Langa," the essential app for reading and listening to the Bible on your own terms. Now featuring Chichewa and English versions. Soon Tumbuka and most of our vernacular languages!

Download it for FREE today on Google Play or the App Store.

Address

Victoria Avenue, Box 740
Blantyre

Opening Hours

Monday 08:00 - 16:00
Tuesday 08:00 - 16:00
Wednesday 08:00 - 16:00
Thursday 08:00 - 16:00
Friday 08:00 - 16:00

Telephone

+265888228722

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bible Society of Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Bible Society of Malawi:

Shortcuts

Share