25/03/2026
Lamulungu likubwerali tikumane ku Hill City Church International kwa Khama ku Machinjiri malo eni eni amene timakumana ndiku Mudzi Motel mukafika pa trading centre pa Khama funsani wina aliyense kuti akuuzeni pomwe pali Mudzi Motel ndipo mukafika lowani pa gate muyende kenako mukalowe pa Khomo la Motel ndipo mukalowa yendani mupite mu Hall. Prophet Ray Harris ndi okonzeka ndipo akufuna kuti azakupempherereni bwerani okonzeka kuti muzandire chozizwa chanu.