Al Noor Islamic Youth club

Al Noor Islamic Youth club Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Al Noor Islamic Youth club, Religious organisation, Bangwe, Blantyre.

Group iyi ndi gulu limene limakhala likuthandiza anthu madera osiyana siyana posayang'anira chipembezo kapena mtundu km gululi lapangidwa ndi achinyamata aku bangwe ku mpingwe gululi lilindi ma busine

01/11/2025

Big shout out to my newest top fans! Fawzan R Dickson

Uthenga oziwitsa ochokera ku Malawi Halaal department
23/03/2024

Uthenga oziwitsa ochokera ku Malawi Halaal department

Al hamudulillah Allah watipanga Kuti tikwanilitse izi
23/03/2024

Al hamudulillah Allah watipanga Kuti tikwanilitse izi

23/03/2024
Apa Àl Noor Islamic youth organization inali pa Bangwe health center
23/03/2024

Apa Àl Noor Islamic youth organization inali pa Bangwe health center

23/03/2024

Asalam Alaykum warahamatullah wa barakatuh

lero Al Noor Islamic youth organization ikhala ikugwila ntchito pachipatala chachikulu dera la Blantyre(queens).

ikakhala kumeneko pamodzi ndi magulu ena osiyana siyana kuphatikiza ndi azanthu ochokera ku ma Radios( Radio islam ndi Angaliba) inshaa Allah

18/02/2024

Announcement @
AL Islamic youth organisations

Bungwe la Al-barakah Charity Trust likudziwitsa makolo komanso anyamata za mayeso olowela mu foundation year kusukulu yosula aphunzitsi ya Assalaam Muallims Training College mchaka cha 2024.

Mayesowa adzachitika malo awa:

DEDZA: Dedza Main Masjid
MULANJE: Albarakah Charity Trust Office (Chitakale)
ZOMBA: ZODEC
BALAKA: Albarakah Charity Trust Office
NTAJA: Ntaja CDSS
MAKANJIRA: Makanjira Main Masjid
MANGOCHI: MADEC
MONKEY-BAY: Aziz Islamic Centre
BLANTYRE: Kameza Training Centre (BDEC)
LIMBE: Islamic Information Bureau
ULONGWE: Ulongwe Main Masjid
NAMWERA: AMA Masjid
SALIMA: Salima Islamic Information Centre
LILONGWE: Islamic Information Bureau
NKHOTAKOTA: Taba Masjid
MZUZU: Islamic Information Bureau
ASSALAAM COMPLEX: Assalam Muallims

DZIWANI IZI:
Ma interview onsewa adzachitika malo onsewa tsiku limodzi.
TSIKU: 24 February 2024
NTHAWI: 08:30am - 12:00 Noon

ZOFUNIKA:
a) Tizithunzi ta Passport tiwili.
b) Copy ya MSCE kapena Copy ya Quran Hifz
c) Darul Uloom Certificate
d) Islamic Studies Intermediate Certificate
e) Osaposera zaka 22
f) Akhale okonzeka kudzayesedwa mmaphunziro awa:
-Qur'an
-Fiqh
-Tawheed
-Seerah
-Arabic Language
-English Language

DZIWANINSO IZI:
Pakutha pa zaka zitatu, sukuluyi imapeleka certificate ya Diploma (Intermediate Diploma of Education in Islamic Studies) kuchokera ku International University of Africa - IUA, Sudan

Mukafuna kudziwa zambiri imbani pa ma nambala awa:
0880262680 / 0994577629

Al Noor Islamic youth organisations

Read Quran
17/02/2024

Read Quran

Allah amadyesa amene wafuna popanda kumuwelengesera Choncho ndi udindo wa Allah yekha odyesa
31/12/2023

Allah amadyesa amene wafuna popanda kumuwelengesera

Choncho ndi udindo wa Allah yekha odyesa

Mwambo uwu aliyense uzachitikira moyo wake pachedwe pasachedwe Oh Allah ndinu mwini wazolengedwa zonse zaupangeni mwambo...
31/12/2023

Mwambo uwu aliyense uzachitikira moyo wake pachedwe pasachedwe

Oh Allah ndinu mwini wazolengedwa zonse zaupangeni mwambo wanga uwu kwa ine kukhala wapamwamba pamaso panu ndipo malipilo ake ndikukhala Hannah yanu yapamwamba

Address

Bangwe
Blantyre
24434

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:00
Tuesday 08:00 - 17:00
Wednesday 08:00 - 17:00
Thursday 08:00 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00
Saturday 08:00 - 12:00
Sunday 08:00 - 12:00

Telephone

+265994197781

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Al Noor Islamic Youth club posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Al Noor Islamic Youth club:

Share