Prophetess NANCY Carlos Ministry

Prophetess NANCY Carlos Ministry God wants to change your life, so follow Jesus

Mulungu ochilitsa.inuso akuchilitseni.
27/08/2026

Mulungu ochilitsa.

inuso akuchilitseni.



26/08/2026

chisomo ichi chisakupitilireni.

Umboni NEBA.

26/08/2026

Congratulations my daughter.

23/08/2026

What physical eyes cannot see, spiritual eyes can see.

Congratulate to yourself God is about to surprise you.

23/08/2026

Ndinawa nenerela kuti akhala ndi mwana wamkazi apa zatheka Mulungu wakwanilitsa mau ake.

Mulungu achiteso ndi moyo wanu.



Inuso ana anu asasowe fees.Pamene mulibe mtengo ogwira Mulungu akutumizireni anthu akuthandizeni.
20/08/2026

Inuso ana anu asasowe fees.
Pamene mulibe mtengo ogwira Mulungu akutumizireni anthu akuthandizeni.



Inuso aliyense amene anasiya kukuthandizani or kuthandiza ana anu Mulungu asowetse mtendere.
20/08/2026

Inuso aliyense amene anasiya kukuthandizani or kuthandiza ana anu Mulungu asowetse mtendere.

congratulations daugh.
19/08/2026

congratulations daugh.

19/08/2026

prophecy confirmation.
Uneneri wakwanilitsidwa.

Werengani inuso Mulimbitsike nao.



18/08/2026

Ndiyakhule ndi iwe amene unakumana ndi amunako nonse muli pa 0 pano nyengozanu zinasitha amunako anachita bwino ndipo sanakutaye paliponse.

Ndikupephera kuti Mulungu apitilize kuwa dalitsa amuna ako.

Address

Chilomoni Center
Blantyre
0992720284

Telephone

+265881110280

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Prophetess NANCY Carlos Ministry posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share