Prophet Ezekiel ANGEL Ministries

Prophet Ezekiel ANGEL Ministries CHRIST OUR KING PROPHETIC CHURCH

BIG NIGHT in   @ COK CHURCHUSIKU wa ULEMELERO. konzekelani🇲🇼🌍🌎
11/10/2025

BIG NIGHT in @ COK CHURCH
USIKU wa ULEMELERO. konzekelani🇲🇼🌍🌎

  Benjamin Ezekiel🎉✨🎉  love you Son✨
17/07/2025

Benjamin Ezekiel🎉✨🎉 love you Son✨

This coming SUNDAY 9am. at COK CHURCH. konzekerani ukuku kuli zapamwamba
12/06/2025

This coming SUNDAY 9am. at COK CHURCH. konzekerani ukuku kuli zapamwamba

Ndinu Wodalitsidwa pamene mukutuluka m'nyumba 🏠🏡 kulikonse mupita ndi mwai
14/05/2025

Ndinu Wodalitsidwa pamene mukutuluka m'nyumba 🏠🏡 kulikonse mupita ndi mwai

SUNDAY service 🏨Kukonza Ubale wathu ndi MULUNGU❤️🍂✨. Okondedwa Pali zovuta  zambiri zimene okhulupilira mwadutsamo,, Mae...
31/03/2025

SUNDAY service 🏨Kukonza Ubale wathu ndi MULUNGU❤️🍂✨. Okondedwa Pali zovuta zambiri zimene okhulupilira mwadutsamo,,

Maesero komanso zolemetsa za moyo zimene zakokera m,mbuyo moyo wanu wa chi Khristu. ena mwagwa, ena mwafooka, ena mukungophupha ndi moyo koma chikhulupiliro chanu chinagwedezeka kalekale.

Lero ndi tsiku labwino lokonzatso ubale wanu ndi MULUNGU. NDIKUKUPEMPHERELANI kulikonse kumene muli 🙋🇲🇼🌏🌍. Mzimu wa MULUNGU ukuthandizeni kubwelera pamaso pa mulungu mwamphanvu🔥⛪.
____________________________________________
MATEYU 24:36 // YESAYA 43:18-19


🇲🇼

YEHOVA ndiwankulu kwambiri😰.Tiyeni tonse tikondwere ndi CHIPULUMUTSO ichi... Anthu ochuluka kwambiri akhulupilira YEHOVA...
15/10/2024

YEHOVA ndiwankulu kwambiri😰.Tiyeni tonse tikondwere ndi CHIPULUMUTSO ichi... Anthu ochuluka kwambiri akhulupilira YEHOVA ndipo ena ochuluka alimbikitsika🔥 .YESU KHRISTU Wapambana🔥🔥🔥...

Ulemelero upite Kwa mulungu... Chifukwa ngakhale ku COK CHURCH mpingo wakula🔥🇲🇼... TIYENI TONSE TINENE AMEEEEEN🙌🙌

We are at chemusa in Blantyre...

0998 70 09 93

  MY WIFE...  Prophetess Ruth Ezekiel.. ❤️. Mkazi wopemphera,,, waukhondo,wosatukwana, waulemu, wozichepetsa, wolimbikil...
08/12/2023

MY WIFE... Prophetess Ruth Ezekiel.. ❤️. Mkazi wopemphera,,, waukhondo,wosatukwana, waulemu, wozichepetsa, wolimbikila, wokongola❤️ koma ine ndikanapanda kumpeza mkazi uyu, sindikanakwatila .

I was young and now I am old, yet I have never seen the righteous forsaken or their children begging bread.  37:25
28/11/2023

I was young and now I am old, yet I have never seen the righteous forsaken or their children begging bread.

37:25

  night,,, Big night,, Big God.31 December Ezekiel ANGEL Ministries
27/11/2023

night,,, Big night,, Big God.
31 December
Ezekiel ANGEL Ministries

Thousands people gathered,,, some were climbing the  ,, just to see me and hear the gospel of Jesus christ,,  today we h...
12/11/2023

Thousands people gathered,,, some were climbing the ,, just to see me and hear the gospel of Jesus christ,, today we have registered hundreds of people as new members of COK CHURCH,,, ONLY GOD CAN DO THIS.. +265998700993.

10 o'clock tikhala tayamba  . MBAYANI PRIMARY SCHOOL GROUND..Chisomo cha Ambuye wathu yesu Christu chikhale ndi ife tons...
11/11/2023

10 o'clock tikhala tayamba . MBAYANI PRIMARY SCHOOL GROUND..

Chisomo cha Ambuye wathu yesu Christu chikhale ndi ife tonse..

Address

Zalewa Road
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Prophet Ezekiel ANGEL Ministries posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share