HCCI

HCCI For more information +265 999 14 83 77/+264 9999 34 744

Zonse zili mchimake tiyeni tikumane ku healing school ku Mudzi Motel kwa Khama ku Machinjiri lamulungu lino pa 17 May 20...
14/05/2026

Zonse zili mchimake tiyeni tikumane ku healing school ku Mudzi Motel kwa Khama ku Machinjiri lamulungu lino pa 17 May 2026 kuyambira 8am. Ili ndi tsiku la machiritso, mamasulidwe, zozizwa komanso chipulumutso. Kaya muli ku Mulanje, Mwanza, Lilongwe, Kasungu, Zomba kaya mumakhala boma lanji bwerani ndipo simuzachoka chimodzi modzi. Mukafika ku Blantyre kapena ku Limbe muzakwere minibus ya Machinjiri ndipo muzamuuze conductor kuti mukatsika pa Khama ndipo mukatsika muzafuse wina aliyense kuti Mudzi Motel ilipati ndipo muzatipeza kumeneko kuti mudziwe zambiri imbani kapena tumizani message pa WhatsApp 0999934744, 0882809010, 0994566544

23/04/2026

KODI HEALING SCHOOL NDICHANI?Healing school kapena kuti Sukulu yamachiritso ndi utumiki wa machiritso wa prophet Ray Harris umene cholinga chake ndikusonkhanitsa anthu odwala komanso ena amene ali zosowa komanso mavuto osiyana siyana kuti aphunzitsidwe mmene angagwiritsire ntchito mau a Mulungu kuti alandire zozizwa, machiritso, mamasulidwe ndi zina zotero mudzina la Yesu Khristu.

Kuchokera pamene Prophet Ray anayamba kupangitsa healing school anthu ambiri akhala akuchiritsidwa kumatenda osiyana siyana monga Khunyu, stroke, misala, ndi matenda ena omwe kuchipatala sankatheka koma atabwera ku healing school Mulungu anawachiritsa kudzera mwa Prophet Ray Harris ndipo anthu amene anali ndi zosowa zosiyana siyana monga kusowa ntchito, banja, kusabereka, mavuto a business, a chuma ndi zina zotero Mulungu anawadalitsa ndipo ali ndi maumboni

▪️Kodi Anthu Amene Amabwera Ku Healing School Amachokera Kuti Nanga Amalipira Ndalama?

Healing school ndiya ulere sitimalipiritsa ndipo anthu amene amabwera ku healing school ndi anthu azipembezo zosiyana siyana ndipo amachokera mmadera ndi maboma osiyana siyana.

▪️Kodi Ndalama Zoyendetsera Healing School Zimachokera Kuti?

Ndalama zoyendetsera healing school zimaperekedwa ndi mamembala a Hill City Church International, ma partners a Prophet Ray komanso anthu akufana kwabwino.

▪️Kodi Healing School Ina Ixachitika Liti?

Ndife okondwa kukuyitanani ku healing school yomwe izachitike lamulungu pa 10 May 2026 kuyambirana 8 koloko mmawa mpaka 5 koloko madzulo. Malo: Mudzi Motel kwa Khama - Machinjiri, Blantyre.

▪️Kodi Mukamabwera
Ku Healing School Muyembekezere Chani?

Mukabwera ku healing school muyembekezere kuzamva mau a Mulungu amene azasintha moyo wanu komanso azalimbikitsa chikhulupiriro chanu ndipo ndipo muyembekezere zozizwa, machiritso, mamasulidwe, kubooleza ndi madalitso. Nonse amene muli ndi chosowa bwerani ndipo Prophet Ray azakupemphererani ndipo Mulungu azasintha nyengo zanu kuti mudziwe zambiri imbani 0994566544

All roads lead to Wala Pvt Secondary School this Wednesday 31st December for a powerful Prophetic Cross over night with ...
30/12/2025

All roads lead to Wala Pvt Secondary School this Wednesday 31st December for a powerful Prophetic Cross over night with God's choice servant Major Prophet Ray Harris don't miss it for anything come and receive your miracle, healing, deliverance, breakthrough, restoration, and prophecy for inquiries please call or WhatsApp 0894729326 see you there

You are specially invited to attend our HOLY GHOST NIGHT OF DOMINION this Friday 1st August 2025 at Wala Pvt Secondary S...
30/07/2025

You are specially invited to attend our HOLY GHOST NIGHT OF DOMINION this Friday 1st August 2025 at Wala Pvt Secondary School in Chiradzulu don't miss it for anything come and experience the power of God there will be miracles, healing, deliverance, breakthroughs, restoration, and prophecy for inquiries please call or WhatsApp 0993 42 53 00

Join God's choice servant Prophet Ray Harris at Wala Pvt Secondary School on Friday 1st August 2025 for a powerful Holy ...
26/07/2025

Join God's choice servant Prophet Ray Harris at Wala Pvt Secondary School on Friday 1st August 2025 for a powerful Holy Ghost Night Of Dominion and your life will no longer be the same again the school is located along Limbe-Chiradzulu road near Chiradzulu Secondary spread the news to your friends and loved ones for more information please call or WhatsApp 0883888490, 0994566544 see you there!

Join us at Hill City Church International this Sunday 13th July 2025 for a power packed Prophetic Sunday Service with Go...
12/07/2025

Join us at Hill City Church International this Sunday 13th July 2025 for a power packed Prophetic Sunday Service with God's choice servant Prophet Ray Harris and your life will no longer be the same again there will be miracles, healing, deliverance, breakthroughs and prophecies you don't want to miss this plan to attend we are located behind Mudzi Motel at Khama in Machinjiri, Blantyre the service will start at 9am sharp for more information please call or WhatsApp 0883888490, 0994566544 Shalom!

CHIRADZULU PROPHETIC MIRACLE NIGHT Join Prophet Ray Harris at Wala Pvt Secondary School this Friday 30th May 2025 for a ...
27/05/2025

CHIRADZULU PROPHETIC MIRACLE NIGHT
Join Prophet Ray Harris at Wala Pvt Secondary School this Friday 30th May 2025 for a powerful PROPHETIC MIRACLE NIGHT come and experience the power of God there will be miracles, healing, deliverance, blessings and prophecy Time:7pm to 5am Wala Pvt Secondary School is situated along Limbe-Chiradzulu road near Chiradzulu Secondary school for more information please call or WhatsApp 0999934744

ALL ROADS lead to Bangwe Day Secondary School Hall (Green Malata) this Sunday 18 May 2025 for a powerful GLOBAL HEALING ...
14/05/2025

ALL ROADS lead to Bangwe Day Secondary School Hall (Green Malata) this Sunday 18 May 2025 for a powerful GLOBAL HEALING SERVICE with Prophet Ray Harris if you are sick and are believing God for supernatural healing, miracle, deliverance or breakthrough then plan to attend this event Time: 8AM to 5PM lunch will be provided for inquiries please call or WhatsApp 0994566544, 0883888490. See you there!

Good NEWS‼️We are xcited to announce that the long awaited event we all have been looking forward to with great exciteme...
10/05/2025

Good NEWS‼️
We are xcited to announce that the long awaited event we all have been looking forward to with great excitement is finally here join Prophet Ray Harris at Bangwe Day Secondary School Hall (Green Malata) for a power packed HEALING SCHOOL on Sunday 18 May 2025 from 8AM to. 5PM come and experience the power of God there will be miracles, healing, deliverance, breakthroughs, restoration, blessing etc for more information please call or WhatsApp 0994566544, 0883888490 see you there!

If you are sick and are believing God for supernatural healing then you need to attend our April Global Healing School w...
23/04/2025

If you are sick and are believing God for supernatural healing then you need to attend our April Global Healing School with Prophet Ray Harris this Sunday 27th April at Bangwe Day Secondary School Hall (Green Malata) don't miss this event because God will do great things the sick will be healed, the bound and the oppressed will be set free, the lame will walk, the deaf will hear, the blind will see if you are trusting God for a baby, job, career or business breakthrough then make assurance double sure to attend for the service will start at 8AM sharp lunch will be provided for inquiries please call or WhatsApp +265994566544,+265 883 88 84 90

Address

Khama
Blantyre

Telephone

+265999934744

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when HCCI posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share