16/03/2024
Ndiyamike Mulungu komanso ampingo Wa Ebenezer popanga promote ndakatulo zanga ndingoti "kumwamba kudyere nyama pansi pano Therere pondiyitana Ku mapephero ausiku wa pa 15 march 2024"AMEN,,,Tinkalinda tere
Zinsinsi za moyo
Ndikufuna bwenzi
Ambuye akukatheni
Dziko lake lomweli .
Ndi zina zambiri..