Prophet Y Simujah

Prophet Y Simujah FAITH IS NOT JUST BELIEVING THERE IS GOD,WE HAVE TO OBEY HIS WORDS.

➖When you hear of wars and rumours of wars know that the end is near {Marko 13:7}.➖Christ is coming sooner than we think...
06/01/2026

➖When you hear of wars and rumours of wars know that the end is near {Marko 13:7}.
➖Christ is coming sooner than we think.🙌

03/01/2026

SUNGANI MAU AWA

➖Kulephera kwanu kwa lero ndicho chipambano chanu cha mawa ngati simufoka mtima.
➖Mwapemphera kwambiri koma sizikuthekabe,ziwani kuti Mulungu akukonza chithu chachikulu pa moyo wanu,nde musafoke.🙌

25/12/2025

NDI ANTHU OCHEPA KWAMBIRI OMWE AMAYAMBA CHI KRISTU NDIKUCHIMALIZA MOYENERA.

➖Ngati munthu sakukwanisa kumvera bwino-bwino Mulungu,amagwa,apo ayi amalowedwa mizimu ya chisocheretso.
➖Timayenera tikhale anthu omvera kwambiri ngakhale mu zithu zomwe sizikutipasa tanthauzo.🙌

➖Mukazaona anthu ena akuyakhula zonyoza ena pa social media osazanyoza nawo Ngakhale onyozedwawo atalakwisadi.➖Satan ama...
04/10/2025

➖Mukazaona anthu ena akuyakhula zonyoza ena pa social media osazanyoza nawo Ngakhale onyozedwawo atalakwisadi.
➖Satan amatha kumpangisa munthu choipa ndi cholinga choti ena anyoze ndipo akanyoza atembereredwe pamodzi ndi ochita choipayo.
➖Kunyoza ena kumabwelesa matsoka patsogolo.🖐️

16/07/2025

PARTNER OYENELA

🌹Munthu Yemwe angakukonde kamba ka maonekedwe ako okha kapena kamba ka zithu zomwe uli nazo,sangakwanitse kukukonda moyenelera m'mene zimafunikila.
🌹Mkazi/Mamuna wabwno amachokela kwa Mulungu. chako.

28/05/2025

KHALIDWE NDILOFUNIKA KWAMBIRI

🌹Ena adati Khalidwe ndi chuma,mau amenewa ndi anzeru kwambiri chifukwa ndaona anthu ambiri akulephera kupeza znthu zabwno kamba kosowa Khalidwe.
🌹Asikana ambiri akulephera kupeza ma banja abwno chifukwa chosowa Khalidwe,ena mwano,ena Kuzikuza,ena chipongwe ndipo ena chifukwa Cha moyo wawo wa social.🙌

MONGOZIWISANABetting,Lotto,Pool and all forms of Gambling is a Sin,Mwana wa Mulungu sakuyenela kuchita nawo zimenezi.🙌
04/05/2025

MONGOZIWISANA

Betting,Lotto,Pool and all forms of Gambling is a Sin,
Mwana wa Mulungu sakuyenela kuchita nawo zimenezi.🙌

➡️ Kupusa kwa munthu kwagona mukusaziwa,tonse tidakaziwa zomwe zili ku tsogolo,bwezi tikusatila Yesu ndi Mtima wathu won...
14/04/2025

➡️ Kupusa kwa munthu kwagona mukusaziwa,tonse tidakaziwa zomwe zili ku tsogolo,bwezi tikusatila Yesu ndi Mtima wathu wonse 🙌.

29/03/2025

KULIKHIDWA KWA MTENGO WAUTALI KU MALAWI 🇲🇼💔

➖Zithu Zina zooneka ngati zosakoma zikamachitika ku Dziko anthu ambiri amangoganiza kuti akuchita ndi satan.
➖Ayi ndithu,Zina zimakhala kuti akuchita ndi Mulungu kuti anthu amphunzilepo kathu {Alape}.
➖Mtengowu mu Dziko lauzimu ndimaona kuti akuulikha ndi Mulungu mwini osati Satan,ndpo Mtengowu wakhala ukupasidwa ma WARNING ochuluka koma udaumisa khosi kamba ka mapangano adziko lapansi omwe udalowa.
⚠️Mtengowu ukalikhidwa anthu ambiri ku Dziko azayakhula zosiyana-siyana zonyoza anthu ena koma omwe mungawelenge post yi musazayakhule nawo chifukwa akupanga izi ndi Mulungu mwini.

12/03/2025

,zimangofunika kumukhulupirira Basi.
Odali Ali iwo amene akhulupirira ngakhale sanaone chifukwa zonse zomwe azikhulupirira zizachitika ndithu.🖐️

Address

Machinjiri Khama
Blantyre

Telephone

+265881340332

Website

http://YSimujah.com/

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Prophet Y Simujah posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Prophet Y Simujah:

Share