Pastor Victor Joshua Mwala

Pastor Victor Joshua Mwala Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Pastor Victor Joshua Mwala, Religious organisation, Blantyre.

18/02/2026

With Prophet Austin Liabunya – I just made it onto their weekly engagement list by being one of their top engagers!

Lero osazilankhulira WEKHA zoipa.Kuli zabwino kunjaku ndipo zoyenera pa moyo wako.Zilankhulire zimenezo.LILIME LIRI NDI ...
13/02/2026

Lero osazilankhulira WEKHA zoipa.
Kuli zabwino kunjaku ndipo zoyenera pa moyo wako.
Zilankhulire zimenezo.

LILIME LIRI NDI MPHAMVU PA MOYO NDI IMFA
Miyambo 18:20-21
Shalom
PJM

M***a kumaoneka osafunikira chifukwa Cha malo amene uli,Kuchoka nkufika pena utha kukhala wamtengo wapatali, komanso ofu...
09/02/2026

M***a kumaoneka osafunikira chifukwa Cha malo amene uli,
Kuchoka nkufika pena utha kukhala wamtengo wapatali, komanso ofunikira kwambiri.
Ziphunzitseni KUSINTHA MALO, mnjira yakaganizidwe NDI kachitidwe kazinthu.
Mwa iwe muli KUTHEKERA KONSE.
Mulungu aika zofunikira zonse mwaiwe.
Masalmo 139:14
Mulungu akupatse chisomo chokadziwa tsogolo lako.
Shalom
PJM

NTHAWI ZINA MAVUTO AMAKUPANGITSA KUGANIZA KUTI PALI CHOMWE WALAKWITSA.KOMA SICHONCHOMULUNGU AKAFUNA KUKUKWEZA AMAKUDUTSI...
07/02/2026

NTHAWI ZINA MAVUTO AMAKUPANGITSA KUGANIZA KUTI PALI CHOMWE WALAKWITSA.
KOMA SICHONCHO

MULUNGU AKAFUNA KUKUKWEZA AMAKUDUTSITSA MMAVUTO KUTI CHIPILIRO CHAKO CHIKUBWELETSERE CHIPAMBANO.

DAVIDE ATAPHA MKANGO, ANAPHANSO CHIMBALANGONDOKUTCHIRE KOMWEKO, NDIPO PANALIBE ULEMU ULIONSE.
KOMA ATAPHA GOLIATI CHILICHONSE PAMOYO WAKE CHINASINTHA.

OSAMAWATHAWA MAVUTO KUMANA NAWO CHIFUKWA AMANYAMUA CHIPAMBANO CHAKO.
Shalom
PJM

05/02/2026
Mulungu akutulutsa MNYENGO zochititsa manyazi.Ndipo akuveka ULEMELERO mdzina la YESU.DZANJA LA MPHAMVU LA YEHOVA LIKUTHA...
05/02/2026

Mulungu akutulutsa MNYENGO zochititsa manyazi.
Ndipo akuveka ULEMELERO mdzina la YESU.

DZANJA LA MPHAMVU LA YEHOVA LIKUTHANDIZA.
OSADERA NKHAWA.

04/02/2026

With Max & Sherry Dine and Lounge – I'm on a streak! I've been a top fan for 3 months in a row. 🎉

03/02/2026
Mulungu akupatse MTENDERE wa mumtima MDZINA la YESU.Zopinga zonse za pamoyo wako zichotsedwe MDZINA LA YESU.SABATA INO U...
03/02/2026

Mulungu akupatse MTENDERE wa mumtima MDZINA la YESU.

Zopinga zonse za pamoyo wako zichotsedwe MDZINA LA YESU.

SABATA INO UKHALA NDI CHIUMBONI MDZINA LA YESU.

Mulungu abwezeletse zabwino zako zimene satana akulanda.Ntchito yako Business yako Banja lakoKatundu wakoThanzi lako Zib...
02/02/2026

Mulungu abwezeletse zabwino zako zimene satana akulanda.
Ntchito yako
Business yako
Banja lako
Katundu wako
Thanzi lako Zibwezeletsedwe MDZINA la YESU
Shalom
PJM

Address

Blantyre

Telephone

+265884442652

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pastor Victor Joshua Mwala posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share