06/08/2026
Wakwiyanso nkhani yoti ndinapepesa kale atawonerana ku mowa
Akometsi ine banjali mwina landikanika kodi ndizingokhalira kupepesa nkhani yoti inachitika kale kale and munthune ndinasintha?
Ndili ndi mwamuna takhala zaka 8 tili limodzi. Koma nthawi ina yake titangoyamba dating ndinapanga cheat. That time I was not sure kuti amandikondadi and amafunadi zoti tikhazikike so I went out with someguy oti anali option chabe incase sizinayende zathuzi.
Atapanga discover tinakambirana and I explained why I had the other guy and I promised him kuti ngati akufuna za serious ndi ine I woukd choose him but I wanted his commitment. He understood and we started dating za serious.
Since that time Akometsi sinapangenso cheat. Not with thag guy or anyone. I have been loyal basi. We started in our life in Blantyre pano tili mu Lilongwe where we both work ine am a teacher.
Komatu basi last month ati he met that man I went out with 8 years. Ndiye kaya ku bathroom ku mowako akukodza ati anawona katundu wa nzawoyo ndiye ali ndi chachikulu chida chakecho.
Munthu kufika kunyumba atakwiya. Kenako wakhalira mafunso opepela kwambiri. After 8 years kumandifunsa ati ndimakonda ma zida zikulu zikulu or zing’ono zing’ono. Kenako ati chida chake ndichachikulu or chaching’oni.
Ine ndikuti ili bwino bwino basi ndi size yabwino, munthu kukwiya mpaka kundiswa mbama ati chifukwa chani ndikumunamiza. Ndiye I had to ask him bhobho mpamene amandiwuza kuti anakumana ndi Ex wanga uja wamuwonera ku mowa akukodza ati ndicha chikulu kwambiri.
Ine ndikuti I chose him not my Ex and it doesnt matter who has a big what I chose him koma no matter what I say akuwoneka kuti wakhumudwa kwambiri and he is not himself dzana wakagula zimankhwala ati zokulitsa chida.
Komatu ali ndi katundu wa size yabwino. Not big, but also not small. And we have two kids together koma panopa he is behaving like someone who has lost self esteem. Eti azindifunsa ati iyeyo ndi adhawo amatha kunyenga ndani? Mmmm
Zabwino bwino izi? Tikhalire zimenezi zowona?