Mawu amoyo

Mawu amoyo Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mawu amoyo, Religious organisation, Malawi, Blantyre.

17/06/2025

Nsanje ndiimene ikulepheletsa ambiri kuchita bwino chifuka nthawi imene amakhala nayo ndiolanga za ena kusiya kupanga zao

02/06/2025

With It's my Sherpad – I'm on a streak! I've been a top fan for 13 months in a row. 🎉

10/05/2025

PAMENE ZILIBWINO THOKOZA YEHOVA NDIPO PAMENE ZIKUONEKA NGAT ZIKUVUTA YAMIKANSO YEHOVA , NDIPO MULUNGU SADZAKUSIYANI CHIMODZIMODZI.

10/05/2025

PEMPHELO ILI LIKUPITA KWA IWE AMENE UKUKONZEKERA KULEMBA MAYESO ABOMA STD 8, FORM 2 NDI WA FORM 4 KUTI NGAT KWANU KULIBE AMENE ANAPHUNZIRA MPATA KU COLLEGE IWEEYOO UKHALA OYAMBA NDIPO NGATI KULIBE ANAYENDETSA GALIMOTO YOU WILL BE THE FIRST PERSON TO DRIVE IN YOUR FAMILY NDIPO ONSE AMENE ANANENERA KUTI SUDZAKHONZA CHAKA CHIMENE CHI ACHITE MANYAZI AYENDA ZOLIZOLI CHIFUKA WAPAMBANA NDIPO ONSE AMENE AMAKUTUMIZIRA NTHENDA PA NTHAWI YOLEMBA MAYESO MUDZINA LA YESU CHAKA CHINO CHOKHA AYALUKE POONA UTACHITA BWINO PA MAYESO AKO NDIWE NYALI YABANJA LAKWANU

10/05/2025

NGATI MULUNGU ANASINTHA SAULO CHIGAWENGA KUKHALA MTUMWI PAULO.
NGATI ANASINTHA MISOZI YA HANA KUKHALA CHISANGALALO.
NDI KUSINTHA SARAI OSABELEKA KUKHALA SARAH OBELEKA .
NGATI NDI MULUNGU ANASINTHA NYENGO ZA YOBU NDI YOSEFE OGULITSIDWA NDI ABALE AKE KUKHALA NDUNA YA MFUMU
LERONSO NDIKUKUPEMPHELERA IWEYO👉👉 KUTI MULUNGU ASINTHE NYENGO ZAKO , ASINTHE TSOGOLO LAKO , ASINTHE DZINA LAKO USATCHEDWENSO MFITI, HULE KAPENA MBALA KUYAMBIRA TSOPANO LINO NDIKUIKIZA MBEWU MWA IWE IMENE IDZABELEKE ZIPATSO ZABWINO KU BANJA KWANU MU MZDINA LA KHRISTU YESU NNAZARAYO NDIWE OPAMBANA , NDIWE ODALITSIKA KOMANSO THANDIZO KU MTUNDU WA KWANU.🙏🙏🙏 I PRAY AND DECLARE IN MIGHTY NAME OF JESUS CHRIST YOU ARE MORE THAN WARRIORS .

CLAIM IT WITH YOU MOUTH

25/04/2025

With It's my Sherpad – I'm on a streak! I've been a top fan for 12 months in a row. 🎉

26/03/2025

With It's my Sherpad – I'm on a streak! I've been a top fan for 11 months in a row. 🎉

15/02/2025

EVERYDAY MAKE GOD YOU FIRST OPTION

13/02/2025

Kuopa chimo ndiye umunthu wa tunthu

13/02/2025

Chiyambi cha nzeru ndiye kuopa Mulungu koma ambiri pano tikumaopa azathu

13/02/2025

Ukamapanga zokondweletsa munthu m'bale wanga uchedwa panga zokomera Mulungu zokha bas

Address

Malawi
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mawu amoyo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Mawu amoyo:

Share