Bishop Moses

Bishop Moses R g

18/10/2023
01/10/2023
07/04/2023

Mau a MULUNGU akafika pa moyo wako moyowo sudzakhala chete kulibeko dzala la mapemphero khala okhulupilika kwa MULUNGU ndipo mu mthwi yake adzakuyankha 🙏🙏🙏🙏

23/03/2023

Dzuro tsilelo dziwa k*t MULUNGU samatsintha ndipo posachedwapa dzitsintha siya kulila ona mayankho ako kwa MULUNGU lelo

15/03/2023

Tien tilape ndik*tsiya machimo pomwepo chiombolo Cha MULUNGU chidzaoneka khulupililan MULUNGU mthawi dzonse mwa muli moyo ndi moyo otsatha

15/03/2023

MULUNGU atikumbukile mu nyengo imeneyi ndipo kumbukilani k*ti MULUNGU mthawi dzonse samakhala chete akumvetsela kulila kwa ana ake

13/03/2023

Moyo wako sukhalanso chimozimodzi pamene MULUNGU aonekele pa nyengo dzako mpomwe umene mwaenela matamando Jehovah

17/01/2023

Kwacha monga mwakufuna kwake dzinali dzotheka otsadzukanso ndi moyo kma wakupatsan moyo ndi cholinga khalani akuchita mau ndipo moyo wanu sudzakhala chimozimodzi mfuneni ndipo iye adzapedzeka muitaneni ndipo adzakuyankhani

12/01/2023

Moyo wanu ndi umboni khalani akuchita mau ndipo simudzakhumudwa MULUNGU adzakhala ku mbari yanu nthawi dzonse mukachita chomukondweretsa amen

09/01/2023

Address

Chiswe Vg Pafupi Nd Namachekecha House
Blantyre

Telephone

+265888526146

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bishop Moses posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share