Ndirande Kachere CCAP Youth Ministry

Ndirande Kachere CCAP Youth Ministry Ndirande Kachere Youth Department

But I will restore you to health and heal your wounds,' declares the LORD, 'because you are called an outcast, Zion for ...
06/06/2026

But I will restore you to health and heal your wounds,' declares the LORD, 'because you are called an outcast, Zion for whom no one cares.'
Jeremiah 30:17 NIV

He said, "If you listen carefully to the voice of the LORD your God and do what is right in his eyes, if you pay attenti...
03/06/2026

He said, "If you listen carefully to the voice of the LORD your God and do what is right in his eyes, if you pay attention to his commands and keep all his decrees, I will not bring on you any of the diseases I brought on the Egyptians, for I am the LORD, who heals you."
Exodus 15:26 NIV

Pamenepo Yesu adalankhulanso nawo, nanena, Ine ndine kuunika kwa dziko lapansi; iye wonditsata Ine sadzayenda mumdima, k...
30/05/2026

Pamenepo Yesu adalankhulanso nawo, nanena, Ine ndine kuunika kwa dziko lapansi; iye wonditsata Ine sadzayenda mumdima, koma adzakhala nako kuwunika kwa moyo.
Yohane 8 vs 12

Muyende mu nzeru ndi iwo akunja, kuchita changu nthawi ingatayike. Mawu anu akhale m’chisomo nthawi zonse wokoleretsa, k...
29/05/2026

Muyende mu nzeru ndi iwo akunja, kuchita changu nthawi ingatayike. Mawu anu akhale m’chisomo nthawi zonse wokoleretsa, kuti mukadziwe inu mayankhidwe anu a kwa yense akatani.
Akolose 4 vs 5-6

Koma inu ndinu mbadwa yosankhika, ansembe achifumu, mtundu woyera mtima, anthu amwini wake, kotero kuti mukalalikire zop...
27/05/2026

Koma inu ndinu mbadwa yosankhika, ansembe achifumu, mtundu woyera mtima, anthu amwini wake, kotero kuti mukalalikire zoposazo za Iye amene adakuyitanani mutuluke mumdima, mulowe kuwunika kwake kodabwitsa;
1 Petro 2 vs 9

Tiyeni Tiyeni!!!Kodi inu simukufuna kupita ku Nyanja? away from noise , kukapanga appreciate nature komanso kukamutamand...
26/05/2026

Tiyeni Tiyeni!!!
Kodi inu simukufuna kupita ku Nyanja? away from noise , kukapanga appreciate nature komanso kukamutamanda Mulungu??

Nkhani ndiyomweyi, Tiyankhuleni!!!

Pakuti kale mudali mdima, koma tsopano muli kuwunika mwa Ambuye; yendani monga ana a kuwunika;Aefeso 5 vs 8
26/05/2026

Pakuti kale mudali mdima, koma tsopano muli kuwunika mwa Ambuye; yendani monga ana a kuwunika;
Aefeso 5 vs 8

Kuti mukakhale wopanda chilema ndi wowona, ana a Mulungu wopanda chilema pakati pa mbadwo wokhokhota ndi wopotoka, mwa i...
25/05/2026

Kuti mukakhale wopanda chilema ndi wowona, ana a Mulungu wopanda chilema pakati pa mbadwo wokhokhota ndi wopotoka, mwa iwo amene monga nyali m’dziko lapansi.
Afilipi 2 vs 15

Inu ndinu kuwunika kwa dziko lapansi. Mudzi wokhazikika pamwamba pa phiri sungathe kubisika. Mateyu 5 vs 14
24/05/2026

Inu ndinu kuwunika kwa dziko lapansi. Mudzi wokhazikika pamwamba pa phiri sungathe kubisika.
Mateyu 5 vs 14

Therefore I tell you, whatever you ask for in prayer, believe that you have received it, and it will be yours. Mark 11:2...
23/05/2026

Therefore I tell you, whatever you ask for in prayer, believe that you have received it, and it will be yours.
Mark 11:24 NIV

Address

Ndirande
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ndirande Kachere CCAP Youth Ministry posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category