06/08/2026
THURSDAY PRAYER AND FASTING
KUMENYA NKHONDO YAMADALITSO PA MOYO WATHU
Munthu wina Aliyense Ali ndi Dalitso wake umene Mulungu anamupatsa kuti ayendemo, koma Madalitso Aliwonse amalumikizika ku Nkhondo imene winaaliyense amaenela kumenya kuti Madalitsowa ayambe kuonekela ku moyo wako, komanso to your Generation.
Genesis 32:23
He took them, sent them over the brook, and sent over what he had.
Genesis 32:24
Then Jacob was left alone; and a Man wrestled with him until the breaking of day.
Genesis 32:25
Now when He saw that He did not prevail against him, He touched the socket of his hip; and the socket of Jacob’s hip was out of joint as He wrestled with him.
Genesis 32:26
And He said, “Let Me go, for the day breaks.” But he said, “I will not let You go unless You bless me!”
Genesis 32:27
So He said to him, “What is your name?” He said, “Jacob.”
Genesis 32:28
And He said, “Your name shall no longer be called Jacob, but Israel; for you have struggled with God and with men, and have prevailed.”
Genesis 32:29
Then Jacob asked, saying, “Tell me Your name, I pray.” And He said, “Why is it that you ask about My name?” And He blessed him there.
Jacob was a man who carried the Generational blessings, but he had to fight with the Angel for the blessing to start manifesting on his life... Akuti pambuyo panali Laban apongozi ake amene amamusaka Yakobo, and kutsogolo kunali Esau yemwenso amafuna Yakobo kuti amalize, koma Yakobo anazindikila kuti nkhondoyi siyaabale anga akundisakawa, Nkhondo ndiya ine ndi Mulungu. Ndipo Yakobo anamuuza Ngelo kuti sindikusiyani Mpaka ntayamba kuwaona Madalitso amenewa. Mulungu anangomusintha dzina ndipo Nkhondo zonse zinatha.
Pamoyo wanu pali Madalitso, koma mwina simukuwaona chifukwa cha Nkhondo zomwe mukukumana nazo, Lero pamene tikusala kudya, Tikufuna timuuze Mulungu kuti "INE SINDIKUSIYANI MPAKA NTAYAMBA KUONA MADALITSO PAMOYO WANGA".
Lero tikulengeza Chipambano pa Nkhondo za :Banja Lanu, Business yanu, Ana anu, School yanu, Mpingo wathu ndi Chilichonse cha Moyo wathu, Ndipo tikayamba KUONA Madalitso a Mulungu mu Dzina la Yesu Khrisitu... Ameni!!