Evangelist Chipi Mandala

Evangelist Chipi Mandala PROCLAIMING THE GOSPEL OF OUR LORD JESUS

26/05/2024

1 Samuel 9 vs 27 ,Ndipo pamene anali kusika polekeza mudzi Samuel ananena ndi Sauli' uzani mnyamatayo abasogola napita iyeyo koma inu muime pano kuti ndikumvese mawu aMulungu.

13/07/2022

Alleluia

Koma Sauli anasunga wamoyo Agagi mfumu ya amaleki ndinkhosa nding'ombe zonenepa.
Aliponso ena lero mwasunga Agagi pamoyo wanu

18/03/2022

Mateyu 24 vs 15
Mukazaona choyipa chonyansa chakupululusa chonenedwa ndi Daniel mneneri chitayima mmalo oyera
Iye awerenga mkalata azindikire

21/01/2022

Pakuti monga kumwamba kuli kutari ndidziko lapansi
Kotero njira zanga zili zazitali kupambana njira zanu,maganizo kupambana maganizo anu "atero Yehova Mulungu"Yesaya 55 vs 9

09/10/2021

People too much bussy brodcast message concerning whatsap and facebook, some people busy do send that to every group and participants abeying that they will be cost much money as they using it because they warned to do so, my question is did you obey God? ,Did you follow his all commandments? Gahena is still waiting for you if you didnt repent ,Luke 12:vs4;I tell you my friends do not fear those who kill only fresh and after they have nothing more they can do. But I warn you whom you can fear, fear him who after kill you has the authority to cast you into hell"yes indeed surey I said unto you fear that" God bless you"

06/10/2021

Miyambo 1 kuyambira vs 28 pamenepo azandiitana koma sindizavomera, azandifunatu koma osandipeza.Amosi 8 vs 11 pakuti akuza masiku akuti ndizatumiza mdzikomo njala osati njala yamkate kapena njala yaludzu lamadzi koma njala yamawu aYehova"atero Yehova Mulungu".Mateyu 24 vs 15 ,ndipo mukazaona choipa chonyasa chakupululusa chonenedwa ndi Danieli mneneri chitaima malo oyera iye amene awerenga mkalata adzindikire "Paulo adalankhula mawu kuti kodi simudziwa kuti muli kachisi waMulungu?,ndimzimu waMulungu ugonera mwainu? Ngati wina wainu aononga kachisi wa Mulungu,Mulungunso azamuononga ndiameneyo chifukwa kachisi waMulungu ali opatulika ameneyo ndiinu*1 akorinto 3vs 16 amene alinalo khutu lauzimu amve chimene mzimu anena"

25/09/2021

Ndipo mukazaona choipa chonyasa chakupululusa chonenedwa ndi Danieli mneneri,iye amene awerenga mkalata azindikire,"nthawi yatha lapani landirani Yesu akhale mbuye ndi mpulumutsi wamoyo wanu"Mateyu 24 vs 15

21/09/2021

Musaope Iwo akupha thupi ndimwazi pakuti akatero alone kanthu kena kakuchita nawo , koma ndikulamulirani amene muyenera kumuopa, taopani iye atatha kupha Ali ndi yakutayani kugehena inde ndinena ndiinu opani ameneyo'

07/09/2021

Sauli alamulidwa aononge aamaleki"1 samueli 15, koma maka vs #9 akuti koma Sauli ndi anthu ena anamsunga wamoyo agagi mfumu ya amaleki ndinkhosa nding'ombe zonenepa koma zonse zonyasa anaziononga konsekonse" allelua"utha kukhala Sauli lero amene umanva uthenga nthawi zonse koma osasintha, agagi wako wamkakamira wamsunga ndimoyo Yehova akuti lapani koma tikuumisa khosi, akuti ndampasa iye nthawi kuti alape koma sakufuna kulapa, okondedwa nthawi yokonza moyo wanu ndiyomweyino agagi wako muononge kuti ubale wako ndiMulungu ukhale wabwino,ambuye akudaliseni"zikomo

01/09/2021

Be repent time is over, behold am near to come and i have a reward to give

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Evangelist Chipi Mandala posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share