14/08/2025
TSIKU 37 LA MASIKU 176 MUSABATA 6 YA MASABATA 25 OWERENGA CHIPANGANO CHATSOPANO (14 August 2025)
ulendo wa m’Baibulo
➡️Muchititse mlubza maso anga ndisapenye zachabe, mundipatse moyo mu njira yanu.(MASALIMO 119:37)
🛐Ambuye, mawu anu amapereka chimene ine ndimafuna, ndicho moyo. Mundithandize kuti maso anga asatanganidwe ndi zinthu zopanda pake koma mmalo mwake akhale tchelu pa mawu anu. Amen.
➖➖➖➖➖➖
🔳Ndime zalero
Marko 14:26-72
➖➖➖➖➖➖
Kodi mukukwanitsa Kuwerenga ndime za tsiku ndi tsiku? Kapena mukumachitanso kuwonjezera, kapena mwina zikumachuluka? Koma ngati mukuwerenga tsiku ndi tsiku ziribwino pamenepo.