Holiness powerful ministry

Holiness powerful ministry This group is teaching gospel

19/06/2022

Walking after the spirit, is placing our faith and trust in the Cross of Christ ROM=8v 1-2

19/06/2022

Kulondola mtanda wa ambuye yesu Christ ndicho cheyembekezo chabwino chonde mulole kuti yesu akhale masters wamoyo wanu

17/05/2022

Yesu akusamalileni siku LA lelo muyende naye mukhale naye akupaseni zosowa zanu akuze malile anu a dani any akhale kunsi kwa mapazi any Amen

09/05/2022

Palibe chosatheka ndimulungu ndaonela pachikhamu LUKA 8:26

06/05/2022

Mzimu wanu uyenela kukhala ndi njala yapemphelo pemphelani mosalekeza kuti muoononge ma plane asatana

10/04/2022

Ndikukulimbikisani musafoke papephelo olengedwa aliyense ndiofunikila pamaso pamulungu tamvelani mulungu akakuonani akukuon monga mtumiki wake chonde tiyeni tigwile TCO yululungu

10/04/2022

But ye, beloved, building up yourselves on your most holy Faith, praying in the Holy Ghost Jude vs.20

05/04/2022

Christ ayenela kumva zowawa posata mapazi ayesu limbikani mtima kufikila chipambano chifika Yesu sachitisa manyazi

03/04/2022

Tapulumuka ndichisomo simphavu sikhondo koma yesu analipila ngongole yauchimo Yesu mukakule

Kodi tingapambane bwanji pankhondo ya uzimu? Munthu opephela ayenela kukonda kusala kudya esitele anasala 3days koma ana...
27/03/2022

Kodi tingapambane bwanji pankhondo ya uzimu? Munthu opephela ayenela kukonda kusala kudya esitele anasala 3days koma anapambana

13/03/2022

Bwanji timadela nkhawa za moyo uno tiyeni tione eksodo 14:14

Address

Chilimba
Blantyre

Telephone

+265995433595

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Holiness powerful ministry posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share