Mavungwe Full Gospel Church

Mavungwe Full Gospel Church Kukonzekera Moyo Wina Watsopano Umene Anauvera Kuwawa Pamtanda Ambuye Wathu Yesu Christu

Masiku otsiliza anayambira pa tsiku la pentecost m'machitidwe Atumwi chapter 2:2 The coming of the Holy Spirit marked th...
25/10/2025

Masiku otsiliza anayambira pa tsiku la pentecost m'machitidwe Atumwi chapter 2:2 The coming of the Holy Spirit marked the beginning of the last days. Koma ndimafuna nditsimikize kuti panopa tili kusonga Kwa masiku otsiliza..
zomwe ananena Yesu zikuchitika tsoka odziwelengera. Wa maso awone ndipo wa makutu amve !
UTHENGA WA KULAPA ulalikidwe ponse ponse.Obisa machimo ake sadzawona mwai koma wakuwalapa adzachitilidwa chisomo.
Madulira alibe ntchito ngati munthu wasochera.

27/06/2025

ECCLESIASTES 11:9-10
REVELATION 22:10-11

In lifetime, you have a right to do anything according to your feelings and heart's desires. But get ready for the consequences.

Be mindful of your decisions, because destiny sometimes comes unpredictably.

What kills us most 😔 is that at the beginning , everything looks good and great to be achieved... but once source and process collapse the destination also comes in different way.

WHAT I MEAN IS YOU NEED TO KNOW WHAT YOU ARE DOING, DON'T LET IGNORANCE USE YOU.
CHOOSE THINGS THAT CAN BE DONE BY YOU CONFIDENTALLY FOR THE SAKE OF YOUR LIFE AND FAMILY.

STAY BLESSED 🙏🎊 IN JESUS NAME.

06/05/2025

Continue you relationship with God until your last breath.

02/04/2025

*"For I know the plans I have for you,” declares the Lord, “plans to prosper you and not to harm you, plans to give you hope and a future."* - Jeremiah 29:11 (NIV)

May this promise from God's Word fill you with hope, encouragement, and faith for the day ahead. Remember that He has good plans for you, and He is always working for your good. Have a blessed day!

30/01/2025

Jeremiah 29:11
For I know the plans I have for you, declares the Lord, plans for welfare and not for evil, to give you a future and a hope.

26/02/2024

*YOUTH*

It is the purpose of the home to maintain the principles and attitudes that must be instilled within the thinking and hearts of young people.
The home is the environment wherein young people are trained for adulthood and to be a benefit to society.
The children of parents submit to the direction of the parents in order that they reflect the spirit of Jesus to the world.

*A.* *The young should manifest the following:*
*¹* Abstain from evil _(1 Thessalonians 5:22)_
*²* Be mature in mind _(Titus 2:6)_
*³* Flee lusts of the flesh _( 2 Timothy 2:22)_
*⁴* Keep law of God _(Proverbs 7:1, 28:7)_
*⁵* Remember God _(Ecclesiastes 12:1)_
*⁶* Be example _(1 Timothy 4:12)_
*⁷* Be enthusiastic _(1 Samuel 17:26-50)_
*⁸* Listen to Scriptures _(Psalm 119:9)_
*⁹* Praise God _(Psalm 148:12)_
*¹⁰* Listen to parents _(Psalm 10:1, 13:1, 17:25)_
*¹¹* Be obedient to parents instructions _(Ephesians 6:1)_
*¹²* Honor parents _(Ephesians 6:2)

*B.* *The young should not do the following:*
*¹* Have evil companions _(1 Corinthians 15:33)_
*²* Despise father's instructions _(Proverbs 15:5)_
*³* Allow others to despise them _(1 Timothy 4:12)_
*⁴* Be self-willed _(Luke 15:11-21)
*⁵* Be disobedient to parents _(Ephesians 6:1)_

*May God bless all Youths and may him guide us until we reach into a better future of spiritually in Jesus name, Amen 🙏.*

_Email: [email protected]_

23/02/2024

Momwemonso chikhulupiriro chikapanda kukhala nacho ntchito chikhala chakufa m'kati mwakemo(( YAKOBO 2 VS 3


Mtengo ulionse umadziwika ndichipatso chake chimodzimodziso Munthu amene amadzitcha okhulupilira Mulungu amadziwika ndi zintchito zake

Chikhulupiriro chopanda ntchito zake mchachabe ndipo mchakufa,Munthu amene amadzitcha okhulupilira Mulungu amayenera kuonetsa zintchito zamzimu oyera zimene zimatsimikiza kuti munthuyudi amakhulupirira Mulungu

Koma lero nzachisoni okondedwa kuti anthu ambiri amene timadzitcha opemphera,amene timadzitcha okhulupilira Mulungu ndamene takangalika kuchita ntchito zonyasa,machimo alitho mwaife, zintchito zathu zikutitsutsa

Okondedwa tiyeni inu ndine ngati anthu okhulupilira Mulungu tionetse zintchito zabwino zimene zingatheso kukopa ena kuyamba Kupemphera chifukwa ngati zintchito zathu sizikhala zolongosoka mkovuta kwa Ife kukopa ena kuti ayambe Kupemphera

Ambuye akusamalireni Nonse. Ameniii 📖🙏📖🙏

23/02/2024

*KODI MA AGENT A SATANA MUKUWADZIWA..?*

Choyamba ndikufuna ndikuuzeni kuti mawu akuti Agenti(AGENT) amatathauza munthu amene amathandizila kuti cholinga(ntchito) cha Kampani kapena Bungwe chikwanilitsidwe mosavuta. Mwachitsazo Aitel Company imadalira ma agents ake kuti ikathe kugulitsa maunitsi ndi ma foni kwa anthu opezaka ku mudzi, m'misika, mntauni, ndi malo ena.

Kunena motsindika Agent ndi muthu ofunika kwambiri chifukwa palibe Kampani yomwe ingakwanitse kugwila ntchito yake mwadongosolo popanda kudalira ma agenti.

Satana nayeso pofuna kuti ntchito yake yopititsa anthu ku Gahena itheke mosavuta komaso mwadongosolo ali ndi gulu la wathu omwe adawalemba ntchito yopititsa patsogolo mchitidwe wa uchimo kuno dziko la pansi

📖 Luka17:1 "Sikutheka kuti zolakwitsa zisadze koma tsoka iye amene adza nazo"

Baibulo pa 📖 Luka 17:1 likutsindika kuti ndizosatheka kumuletsa Satana kubweretsa ma uchimo kuno kudziko ali ndi tsoka anthu omwe amathandizira Satana kugwila ntchito yopititsa anthu ku Gahena.

MA AGENT ASATANA ALIPO MITUNDU IWIRI ⬇️⬇️:

(i)** Unregistered Satanic Agents

Ili ndi gulu la anthu omwe Satan anawalemba ntchito yothandizila kupititsa patsogolo m'chitidwe wa uchimo koma anthuwo eniake samadzidziwa kuti Satana adawalemba ntchito yopititsa anthu ku Chiwonongeko. Ankhristu ambiri otembenuka mtima ali mu gulu limeneri la ma Unregistered Agents, tsiku ndi tsiku akumuthandiza Satana kuchulukitsa uchimo komaso kutengera ku anthu Gahena koma zachisoni iwo samadziwa kuti adalembedwa ntchito ndi Satana.

(ii)** Registered Agents

Mu gulu ili ambiri ndi Ziwanda komaso anthu amaudindo akuluakulu ku Satanic, Azibusa ochokera pansi panyanja(False Prophets) ndipo ma Agents amenewa kwa iwo kumutumikira Satana imakhala ngati ntchito yawo moti amalandira ndithu ndalama pa mwezi(salary and benefits). Gulu limeneri ndi loopsa kwambiri chifukwa amachita kupatsidwa target(mulingo) oyenera kutengeredwa ku Gahen pa chaka...... *(continue.......)*

*Gift Kaunga Nyirend

23/02/2024

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Chipiliro Mwale, Don Fik

11/09/2023

I went to a new restaurant that had just opened in my neighborhood cos I saw their free WiFi advert for all guests.

I asked the waitress for the password as I was ushered in.. She told me, eat first!

Without arguing, I smiled and placed my order for food and drinks and when the food was being served, I asked for the password again... and the waitress told me again... eat first!

Of course I needed the password while waiting for my food to be served so I could catch up on some work emails and social chats.

Now that I'm almost done eating, I wonder if it really makes sense asking for the password... but I still went ahead to ask the waitress again.

"Please, what's the password?" I asked, and the waitress told me eat first.

"But I have finished eating my food!" I responded angrily.

"No sir..." she said... "That's not what I meant... the password is actually *eat first* all in small letters".

At this point, I wasn't sure whether to laugh or get angry.

Pay attention to every spoken words, within it may be the answers you've been looking for.

Ponder on this.

Address

Mzimba

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mavungwe Full Gospel Church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Mavungwe Full Gospel Church:

Share