Utumwi Senga-Bay Section Malawi Assembles of God

  • Casa
  • Peru
  • Lima
  • Utumwi Senga-Bay Section Malawi Assembles of God

Utumwi Senga-Bay Section Malawi Assembles of God Chonde apa futsani zomwe mukufuna kuziwa za utumwi kapena za moyo wa uzimu komatso za kutembenuka m'

Mulungu samataya ake kwalero titanena moteromu.
11/11/2020

Mulungu samataya ake
kwalero titanena moteromu.

24/07/2020

Kodi piano ndiye tikutani pozindikira kuti tsiku lirirotse liri ndi zovuta zake . choncho tisakhale awulesi mumachitidwe athu.

07/02/2018
04/02/2018

TEACHING ABOUT SALT AND LIGHT

MATTHEW 5:13 -16
13 "YOU are the salt of the earth . But what good is salt if it has lost its flavor ? Can you make it sailty

03/02/2018

Tiri ndizotani 2018 mumadera mwathumo? komatso chaka chino tiyeni tiringarirekotso mozama kupotserako chaka chapitachi. Kwatsalaku tisagoneso

14/01/2018

Achibale tiyeni tiyende ndi utumwi muchaka ichi cha 2018 tinene zowona apa chaka chapitachi sitinamalize bwino ma utumiki athu, Azitsogoleri apa tichedwepo komatso mapemphero achitike mwamadongotsolo abwino osamakhala ngati mozizimukira tiyeni tigonjetse zoyipa pochita zabwino pozindikira kuti ano ndimatsiku otsiriza

20/10/2017

Zachuma tisaziyetse ngati ndizoyamba tayiwala zakulalikira madera osiyana siyana, mipingo yasiya kukamba za utumwi koma ndalama zalowa zingati? Sizolakwika ayi koma tiyambe zoyamba zikhale zoyamba awonjedza abale awa Atsogoleri wakuphompho uwu maso ali nawo koma sakuwona

02/08/2017
02/08/2017

Antchito achepa, zokolola zachuluka : Mwachindunji olalikira uthenga wa yesu akuchepa, koma ofunika kuti atembenuke mtima aķuchuluka , tsono tipemphe mulungu kuti atiwonjezere anthu oti azitumikira. Choncho penyani mmene mukuchitira kwanuko achuluka ndi atiwo?

06/02/2017

2017 Tisakhale chete abale kopanda chotitsusa?

Dirección

Senga-bay Sa
Lima

Página web

Notificaciones

Sé el primero en enterarse y déjanos enviarle un correo electrónico cuando Utumwi Senga-Bay Section Malawi Assembles of God publique noticias y promociones. Su dirección de correo electrónico no se utilizará para ningún otro fin, y puede darse de baja en cualquier momento.

Compartir